uwu ndi umboni oti ndalama ilibe phokoso...anthu andalama Ali chete koma mkavunyani ngat ine koma phokoso 🤣🤣@kech salon kamunthu kaja ndi aka umandifunsa pa mikozi kaja
2024-07-02 16:45:32
1
victornottah :
Iwe nde ndi mbuzi ya mwana ndithu Bola apapa moyo waudziwa😂😂😂
2024-07-02 14:19:57
1
thamikomemoC :
indee😂💔
2024-07-02 12:11:46
1
myabamary :
amayerekedwera zinthu zoti sizakenso 😂😂😂😂
2024-07-02 09:44:05
1
usersitibeib :
Lero matama onse balala
2024-07-02 07:32:47
1
userlara punja :
Kkkkk nyamata zamuonekela uku akukwela galimoto yaulele ya boma