@brenda_dzanja: CHILEMA ATAYIDWA PA DZIWE: Chifukwa chokula mchombo ____ Zinthu izi ndi zoti zimachitika ndithu mmakwalalamu. Makamqka kusalana chifukwa choti wina Ali ndi olumala. ______________________ Nthano ndiye zilipo zambiri ndithu koma nthawi ndi imene ikumachepa🤦🏾♀️ #malawitiktok🇲🇼 #zambiantiktok🇿🇲 #brendadzanja
Brenda
Region: MW
Friday 06 December 2024 18:44:57 GMT
Music
Download
Comments
Dj_Kankhwani 🇲🇼 :
iwe Bulenda😅 ukufunika award
2024-12-06 19:51:15
37
witness :
aunt mumandikumbutsa nthawi imeneyo Mai anga akundiimbira nthano zinali nthano zopunzitsa chikondi Cha pa ubale ndangoisowa nthawi imeneyo 🥹
2024-12-07 05:34:46
9
mercymwagomba :
umàtha Mamie
2025-03-04 04:55:28
0
Charles Joseph :
umathaa brenda ulmuu wakoo. watiphuzitsaa app thank you
2024-12-11 10:11:11
8
Banda :
😂😂😂ndaphunzilapo kena kake Loma uli ndi luso keep it up 💕💕
2024-12-07 14:31:57
10
photo :
pitilizani
2025-03-06 11:49:18
0
user ireen :
zili bwino kwmbiri 💖💥
2024-12-07 17:08:16
3
mariam George 1919 :
Nice Brenda
2024-12-06 19:55:15
9
Shee :
koma umakamba tinkhani tokhudzatu,,taphunzirapo🙏🙏
2024-12-07 17:01:13
4
Maggie Chidakwa :
umakwana dear zimaphuzitsa🥰
2024-12-06 19:28:41
8
Dimitri don :
this is cool impacting something in this generation 🤗🤗🤗😊
2024-12-14 04:05:15
3
Aida Jesman :
kom eeee tapuzira zambiri 🙏🙏
2024-12-07 04:50:23
4
Janet lungu :
so interesting 🥰
2024-12-07 06:43:57
6
makechichi :
agogo akuchimuna or akuchikazi asking for a friend
2024-12-07 12:07:04
6
Mary Chongo :
sending love from Zambia ❤️❤️
2024-12-07 08:49:04
4
Josophine Gawani :
very nice dear
2025-01-31 16:38:45
1
Brendah Harrison :
Sending hugs 🫂 🥰🔥
2024-12-07 13:17:41
4
miss Khoza💕 :
nice one😘
2024-12-06 19:29:11
5
youngchimenya :
ap speechless nice story
2024-12-07 21:28:36
4
user7695905314406 :
umatha
2024-12-06 19:31:08
5
To see more videos from user @brenda_dzanja, please go to the Tikwm
homepage.