@kaykaydawa: Lilongwe

kay kay dawa tha legend
kay kay dawa tha legend
Open In TikTok:
Region: MW
Tuesday 25 February 2025 10:40:54 GMT
15433
478
147
112

Music

Download

Comments

user3771774003357
Babina🥰💝🍷🍾 :
this is worse than what peter went through kkkkk mulungu si jemusi
2025-02-25 19:47:43
19
user9327862782066
VILLAGE CHAMPION :
lero ngati sinditukwana landlord ndimwayi simomwe ndakondwera
2025-02-25 18:36:07
13
mugodemavuto
mugodemavuto :
Lero zatheka bwanji osakumana ndi adzikwanje?
2025-02-25 20:02:50
5
tipulike
Tipulike :
lelo zakubwelaniso 🤣🤣🤣🙌adad my vote
2025-02-25 17:30:25
9
taddytadz.j
Taddytadz.J。♡ :
true definition of adani ndi omwewa timaseka nawo wa😂😂😂
2025-02-26 06:10:50
3
user9084426018707
user9084426018707 :
awa ndi ma demo opanda date oyambika okha okha. that is what we call kutopa Kwa a Malawi they will not need anyone kuti awauze date amangotopa kenako
2025-02-26 11:56:32
1
funny_md1
funny_md1 :
ndadandaula ndinayenda opanda legeni😩
2025-02-26 06:42:56
2
user3104778196181
user Mariana :
Apolice nawo anangofika pomangoona 🤣🤣🤣
2025-02-26 06:05:43
1
vosteorq7wi
VOSTER :
Guys when was this?
2025-02-26 10:01:05
0
user7035712122277
Autly :
even a police wo akuimba nawo mu ntima kma sangakuwe🤣🤣🤣
2025-02-26 09:33:19
2
emilynyasulu
Emily :
Lazalo wa watilephera 😳😳😂😂 galu uyu
2025-02-26 03:45:52
2
user19911465870228
Ûñ Qqùàvò36 :
apa anthu aku Lilongwe ayamba kuchangamukatu😅
2025-02-25 20:54:33
3
gibo893
Gibo :
Olo azikwanje anadziwilatu kuti akayesela zachibwana zawo zinja atibulidwa kwa mnanu🤣🤣🤣🤣
2025-02-25 23:22:33
1
sakajam6
James monemen :
yanditengela nthawi kuti ndimve abusa onyenga chilungamu kuti Kha 🤣🤣🤣
2025-02-26 00:09:27
1
user8188009537344
James :
achina boma ndilomweli nawonso avomeledza kut chikangawayi ND nyapapi
2025-02-25 18:42:41
1
user731764911837
Jack the girl :
Simene kumalili 🤣🤣🤣🤣
2025-02-25 17:59:50
1
To see more videos from user @kaykaydawa, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About