@bigsmallzjr_anjobvu: Lero ovutika si ine mwina mawa kapena nkuja 😂😆🔥🔥.. za mafana oweneka bhoo 😊🥴🔥👑🐘#viral #fyp #tiktokviral #anthuntomwefe #tiktokzambia🇿🇲 #tiktokmalawi🇲🇼
Anthu adzadza ndima comment awu mphawimphawi... Aaaah! this is just content Anjobvu amabhebhetsa koma😂🔥🔥🔥
2025-06-06 07:27:22
40
susannamanja :
Mr Chidandale, I love your confidence, inu mumabwela pano kuzapanga zanu ndipo simunyoza munthu...ndipo mumaoneka kuti you enjoy what you do. Please don't waste time responding to anthu amakunyozaniwa...musamavutike nkuwatukwana. Do your thing basi and enjoy your life. Onyoza onse block them. Ife content yanu imatiwaza..inu ndi good vibes man...
2025-06-09 07:32:45
16
monica 💖🌹🔥 :
Ona iweee zipwisi madzi madzi
2025-06-08 21:27:38
4
khady1748 :
I have to use this sound mawa👍😂
2025-06-04 16:44:36
15
Timale✨ :
" Diyoooooooo nkhangatitu"😂😂😂
2025-06-04 15:42:36
48
Molly :
This kind of confidence will annoy the insecure dudes n girlies😂. lemme use this sound mwee🥳