@kuyapodcast: Kodi Kuya Podcast ndichani? Kwa kanthayi, mwakhala mukuona zimene takhala tikumayika patsamba lanthuli, koma lero tafuna titsindike kuti Kuya Podcast ndichani. Motero, joyinani tsamba lathu la pa WhatsApp kuti mutsate zambiri za Kuya, ndikupereka mafunso kapena ndemanga zanu. Tiyeni aMalawi tigwirire ntchito limodzi, pofuna kusintha ndikutukula dziko ndi mtundu wathu. Lowani patsamba lathu la WhatsApp: https://whatsapp.com/channel/0029VadR4roGufJ5Wg8LDA2Z #kuyapodcast #politicsandfinance #drmcbridenkhalamba
kuyapodcast
Region: MW
Thursday 02 October 2025 07:08:05 GMT
Music
Download
Comments
Christopher Chipingasa :
next big deal 🤝
2025-10-02 11:33:32
2
Jolam Makondetsa :
following
2025-10-04 08:34:43
0
Danida :
Bwana president 🔥
2025-10-03 04:12:09
0
alfred George :
my vote
2025-10-03 04:16:46
0
Tawonere Zinyongo :
bwana president 2030
2025-10-02 19:24:04
1
To see more videos from user @kuyapodcast, please go to the Tikwm
homepage.