Koma mukulu uyu , the way he is articulate things. ndiwa nzelu
2025-10-15 03:38:19
11
Tolani Kondowe :
ili ndibodza when it comes about nyambo yophera shark. I have been in fishing in Atlantic Ocean for a period of time and nyambo yophera shark ndi tuna heads . shark head does not have gold, the most expensive part of shark ndi fins mutu amangotaya ndiye asatinamize ,amafuna ziwalo za anthu kamba kankhani Zina not for fishing