@ifeyondiifeyospace: Lero kwachema ndi kuno kusukulu yaukachenjede yotchedwa Malawi University of Science and Technology (MUST) komwe kukuchitika zija amat VC trophy 🏆 Apa ndipa Ecowater Ndata store pomwe Pali sound yachabe Kwambir komanso ku MUST stadium kulinso masewelo osiyana siyana