@janiechilaka209: Mulungu Akuti mulape siyani kudzikongoletsa

pastor Janie ndeule
pastor Janie ndeule
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 17 May 2026 05:07:51 GMT
24741
730
144
166

Music

Download

Comments

maggie.k.chioza
Maggie k chioza :
ine kudabwatu kut why masiku ano ndimadana ndikuphoda??? ndinali munthu mmodzi oti sindingayende pansewu osaphoda, koma ndikunena pano ndinasiya kuphoda osati kut sindifuna koma ndimamva kutsutsika mmoyowu , 😭😭😭😭😭😭 ambuye apitilize kundisintha muzambili
2026-05-17 18:33:30
6
gracemwazimva
i-grace :
Kumanga tsitsi lokhalokha ndintchimonso kodi
2026-05-18 04:52:12
2
ellenwanyeta
ellen Wanyeta :
amen this is true mammie
2026-06-14 23:25:49
0
memorymwenda950
Memory Mwenda :
komanso Kod tikapita kwazungu vesi ili lovala matrouser limatanthauzidwa Motan ndithandizen
2026-05-19 02:02:03
1
user4763630539014
E.ZULU :
Anthu ambirife uthenga uwu timauzemba. AMBUYE atithandize ndithu 👏👏sindikudziwa pano chifukwa chani ndinameta n zophodazi nde zikuvutaso kwambiri.gogoda nde ukuvuta kusiya AMBUYE andithandize
2026-05-20 13:47:11
5
joseph.kachepa
APOSTLE J.W KACHEPA :
Anthu akuona ngati masewera,komano sakudziwa kuti nthawi yatha.......🙏🙏🙏
2026-05-18 06:01:41
3
sophiekhomera615
sophiekhomera615 :
God bless you mama
2026-05-18 20:57:45
2
chashe140
Nohala :
Ndizinthudi zowawa kwambiri kumaona ngati iweyo pa dziko pano wapanga zabwino pomwe Kwa Mulungu sizili choncho😭
2026-05-18 08:59:13
3
fannyjemus
fannyjemus :
kumvala gogoda ndi ntchimo
2026-05-17 17:56:57
1
user6631126082018
Omake fefi :
mumandisangalatsa mami ndife achinenero chimodzi.
2026-05-17 08:08:58
2
user4228519656228
VESSEL OF GOD :
Amen 🙏 Mulungu akuze malire Anu mtumiki
2026-05-18 21:30:01
1
user203625209145207
memory zimba :
koma mau awa sikuti ndi azimayi azibusa kapena azibusa achikazi okha yai koma kwa aliyese wokhulupilila wamkazi
2026-05-19 04:41:42
3
nyamwale.blessed
Masautso Blessings Nyamwale :
Mukundimvekera Chi Kasungu kapena Nkhotakota
2026-05-18 08:50:45
1
judithmoffat886
miss judah :
powerful massage
2026-05-26 17:54:03
3
lucy.lucy058
Lucy :
amen and amen ccter
2026-05-17 16:03:39
1
user508811904051
happ :
congrats and great massege very big Amen.
2026-06-05 15:22:38
1
user7334726851458
a,bu.le mw (villah) :
powerful message
2026-05-17 19:26:05
1
user7856985948704
felister :
Amen mamie
2026-05-26 11:39:22
1
leahmtengezo
Leah Mtengezo :
Amen
2026-06-03 04:53:19
1
user4729185952428
user4729185952428 :
Amen ambuye atithandize
2026-05-17 15:40:21
2
levigerald175
Levi Gerald :
amen mawu amphavu
2026-05-17 18:11:35
0
licieagold
Licieagold❤️💓 :
Amen and Amen
2026-05-24 04:09:10
1
hassanmackintosh
M HASSAN PRASAD :
zoona
2026-05-23 05:03:38
1
elizasosten1
Eliz mphatso Sosten :
Amen
2026-05-22 10:19:53
1
anne.kalipo
ANNE KALIPO :
Amen chilungamo mamie ,Ambuye akudalitseni 🤲🙏🙏🙏🙏
2026-05-25 11:39:48
1
To see more videos from user @janiechilaka209, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About