@prophethinoskamanja: Replying to @cnartantony #malawitiktok🇲🇼 #zambiantiktok🇿🇲 #mozambique🇲🇿 #southafricatiktok🇿🇦 #tanzaniantiktok🇹🇿

MAJOR PROPHET THINOS KAMANJA
MAJOR PROPHET THINOS KAMANJA
Open In TikTok:
Region: MW
Saturday 13 June 2026 07:38:01 GMT
40452
1935
596
794

Music

Download

Comments

user51542952175363
martha phiri :
Koma ife dzidzatichitikira izi ife😭
2026-06-14 05:24:32
0
yankho049
yankho :
amene angapezeke number yao please share
2026-06-14 05:44:25
1
bridgetchamamuson
bridgetchamamuson :
amen and amen 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
2026-06-17 21:29:29
0
user1440485025046
user1440485025046 :
mundipemphelele mamuna wanga alipawulendo mawa kupita kumalawi kukapanga passports akayende bwino
2026-06-17 20:41:07
0
ellenbanda191
Ellen Banda Patrick :
munthu wa Mulungu bsns yanga sikuyenda komaso ndikudwala mzipatala ndayenda koma machilitso eni eni sakupezek help me pls
2026-06-14 19:23:04
0
user1631361813562
user1631361813562 :
Ineyo ndikumalota zoyipa daily anthu okufa komanso moyo wanga ukumakhala wa khawa nthawi zonse
2026-06-15 00:32:29
0
diana.mumba.phiri
Diana Mumba Phiri :
a prophet nyengo imeneyo ndiyanga, business yanga sizikuyenda, chilichonse chayima , mzimai wamasiye ndisowa wapemphero anu
2026-06-14 11:33:52
0
user1236310000784
user1236310000784floh beib :
ambuye mundichitile chifundo mamuna anangondinamiza kt azaonekera mpaka pano kuli ziii mundipulumuse ine
2026-06-14 05:44:47
2
muderanjibanda
FMB2 :
a prophet mundipemphelereko ndibwelere ku ntchito komaso ndufuna mwamuna akhale ochita chifuniro cha mulungu
2026-06-14 04:20:29
2
buli3908
Buli :
Amen and Amen 🙏 zichitike paine please ndingokhar osagwir ntchito
2026-06-13 08:03:30
2
patriciakamanga46
Patricia Kamanga :
Bola muzitilalikila choncho ndawakonda mau anu osati zija zothamanga
2026-06-14 15:40:01
1
user6205158773765
judie0 :
amen
2026-06-13 07:52:06
2
user8713854510208
Chifundo Guta :
Amen Amen Ameeeeeeeeeeeeeen 😊ndakhulupila
2026-06-13 18:42:52
1
user7008323662248
triza :
Kodi mumatani kuti zitelo😭😭😭
2026-06-13 18:23:02
1
ullitermapando8
Ulliter Mapando :
amen
2026-06-13 07:58:16
1
khefado6
Khefado :
amen nanenso machilitso mulungu andiyendere
2026-06-17 20:12:11
0
user78527942846028
folomina :
mulungu tulukilani pa moyo wanga
2026-06-17 20:24:49
0
ruthmsiska478
Ruth Msiska :
ntchito sindikuyipeza Mulungu andichitire chifundo
2026-06-16 02:17:25
0
jazzfrank0
juhailah 🇲🇼 :
ameen🙏
2026-06-13 08:16:25
1
user5715920237976
cute pie :
ndkufuna ndichite bwno maphunzilo angaa
2026-06-13 07:43:14
3
nomsaphir1
Elsa :
a prophet ndipepheleleni ndufuna mamuna zungu ,akudawa andipha ndi BP
2026-06-13 08:39:25
2
patricla.paudala0
Patricla Paudala :
amen abuya ndichitileni chifundo
2026-06-13 17:33:47
0
user5674113328493
velonica :
amen and amen zichitike pamoyo wanga business yanga suyuyenda
2026-06-13 09:07:36
1
desmondfrank419
Desmond Frank :
mundipempherere ndikufuna tchito ya nyumba komano yoyendwla mudzina la yesu amen
2026-06-13 09:22:26
1
thoko.kalulum
thoko kalulum :
Amen and Amen
2026-06-17 19:46:04
0
To see more videos from user @prophethinoskamanja, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About