ndikufuna ndipeze business yabwino komaso banja la bwino aman and amen
2026-07-01 05:03:24
3
user92912501319666tadala :
ndikufuna business yanga yamadzi ixiyenda kwambiri komaso mwana wanga faith ambuye amumasure ku miximu yoipa
2026-07-14 19:06:55
1
Omega Mwamphashi :
Gratuity peace word of God. Amen
2026-06-27 08:15:45
1
maureenphirih :
zisomo zochuluka pamoyowanga pa business tanga pabanjalanga amen🙏
2026-06-18 20:00:34
7
merisha :
murungu ayendere nyengo zanga papa siziri pabwino 🙏🙏
2026-06-19 14:57:11
2
Alinafe Anord :
Amen ndkufuna murungu atsegure kuyenda kwa business yamunanga kmaso kutseguka kwa ma plan pa aja pathu komaso kutheka kwachithu chomwe tapanga cz zimangothera mjira chirichose chomwe tapanga