@sha.qeel: Kuchoka kumudzi 2009 Kupita Ku South Africa 🇿🇦, kubwelera panyumba 2026 🇲🇼 Koma chochita kuthamangitsidwa ndi xenophobia, nkukapedza panyumba banja lidabalalikapo 😢 nkuyambiranso pa 0... AMalawi tiyeni tidzikumbukira Ku mudzi 🙏 kwanu ndi kwanu Kwa eni kulibetu nkuwo! Pangolin Lai mw