@pangolinlaimw: #malawitiktok🇲🇼 #southafricatiktok🇿🇦 #zambiantiktok🇿🇲 #tiktok

Pangolin Lai Mw
Pangolin Lai Mw
Open In TikTok:
Region: ZA
Wednesday 24 June 2026 19:25:55 GMT
52172
1344
169
105

Music

Download

Comments

user132518032173
Lucha :
man koditu anthu anatawa kumalawi chifukwa cha mcp anawononga ziko .after zaka 5 ndipamene anthu kumalawi anatawa kupita mayiko akuja.mcp muzaka 5 njala komaso kusowa kwa ndalama ndi kudula kwa zindu.
2026-06-25 08:21:20
5
jane.wa.maluwa
jane wa maluwa :
Namalomba chisilu chamunthu ngati chimenechi nduna yopanda nzeru zibambo osalowa madzi
2026-06-24 19:40:27
12
user7588249161752
lovemore Mangani :
pray for him to have lv over his national, do not hate him please, god must forgive him
2026-06-27 02:24:20
0
user16015395217004
Gamango G :
Ayi akulu Inu ndinu aboza kwambiri Munthu uyu akamalankhula amasata malamulo osati zofuna amalawi omwe Ali ku Jon ayi Inu enafe siokhumudwa
2026-06-25 06:50:09
2
kelvin.gonthi
Kelvin Gonthi :
panyelo pako napantumbo ameneyo machende otupawo
2026-06-25 02:26:04
1
lameckbanda857
Lameck Banda :
dpp woye mwayamba kudziwana zikhalidwetu kkkkk muthana nokhanokha
2026-06-25 04:38:18
6
fatima.willo.nami
Fatima willo Namiyaka :
mmmm sanayakhule bwino
2026-06-27 04:43:51
0
zhoulf2
Zhoulf :
What is your point bra? Mukunyoza achimwene mwinanso tinene kuti mukutukwana. Don't include everyone. Iam not related to Namalumba koma mwaonjeza ngatinso momwe analankhulira Namalumba. I think this is personal. Apa tinene kuti inuyo mukuthandiza kapena mwabwera kuzatani? Anyway it's your thinking bra
2026-06-25 07:06:04
1
chirwamponda1
Chirwa Mponda :
Zaziiiii wakumana nayo cadet mzako
2026-06-25 02:30:24
1
yohane.wilisoni
YOHANE WILISONI :
galu wamuthu
2026-06-24 20:05:49
3
lovenes.lovenes
Lovenes Lovenes :
Ndioyipa
2026-06-25 02:01:31
3
user4561757921910
iamjusthere :
Uyuyu sanayakhuledi bwino chisilu chamunthu 😥😥
2026-06-25 14:18:51
1
henrymalunga6
henrymalunga6 :
Uyuyu zinangovuta kuti anapatsidwa udindo umenewu koma samatha kuyankhula zogwila mtima ndipo kunkuyu anali dolo idziwa kuyankhula
2026-06-25 04:17:42
3
moffatlector
Godfrey :
mmutu mwa namalomba muli madzi okhaokha, ndi zokayikitsa ngati ali ndi bongo
2026-06-25 08:13:05
1
richmankondowe400
Richman Kondowe :
andale awa amatifuna nthawi yovota amabwela ngat abwino taonan pano aiwala
2026-06-25 05:43:32
2
bandaflaming
flaming Jim👾 :
Tell him bro👍👍
2026-06-26 22:00:04
0
carlos15th0
AGAMAH💪🔥🩵🥰♥️🫀💝🇲🇼🇿🇦 :
yes good 👍 good talking loudly
2026-06-26 07:00:55
2
waykmw1
WAY K MACHINGA BOY :
umakwana bro❤ 🙏🙏
2026-06-26 18:25:36
0
kelvinmwikhoma
kellsMW😎 :
kumkuyu uja ndidolo,kuyankhula amatha,,vuto ndiboma lomwe amayankhulira,,,koma nyamalombayu ndi phala leni leni
2026-06-25 03:14:52
5
dejema5
Dejema :
yeti kuno anthu akuphedwa nkumatinso chitani nawo iìiiiiiiiihhhh ambuye awakhululukile sure
2026-06-25 07:37:06
1
moffatlector
Godfrey :
Mutu umenewu muli zero pa 10, akadakhala Moses Kunkuyu akadalankhula za NZERU. Umuuze galu ameneyi.
2026-06-25 08:11:07
1
richard.gawani3
Richard Gawani :
Wayankhulako zanseru ❤️❤️
2026-06-25 10:51:03
1
0601363270jeke
Alfred :
inde zoona ndi munthu oyipad Mmmmm kuchita kuwapeleka anthu kt anthamangitsidwe mmm
2026-06-24 20:48:57
1
chikondinyongo
CHIKONDI CHA NYOO :
achoke ndiozi konda yekha
2026-06-24 19:47:02
2
user8670791011188
sifat :
Boni kalindo atithandize kutukwana galuyu
2026-06-24 19:55:09
2
To see more videos from user @pangolinlaimw, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About