@jnw.nyasaland.off: Asilamu ndi amene akhala akuthandiza a Malawi amene ali pa camp ku South Africa Akuti akhrisitu mumalalikila za chikondi komanso anthu azipeleka chakhumi koma simukuwonetsa chikondi Akutero Dr Namadingo #fyp #facebookreels #fypシ #malawitiktok🇲🇼