@manupage09: #malawinewsupdates🇲🇼

MALAWI NEWS UPDATES
MALAWI NEWS UPDATES
Open In TikTok:
Region: ZA
Tuesday 14 July 2026 09:52:12 GMT
72224
1928
240
168

Music

Download

Comments

harie.54
Harie 54 :
ineyo zikundivekela ngati a Lapukeni amadziwa mission yonse koma kuti amasuke awauze akazi awo chilungamo amaopa
2026-07-14 16:54:12
3
jeannet154
Jeanette :
Amayiwa apaseni chitetezo chokwanira ali ndi zambiri zofuna kugawana nafe.
2026-07-14 19:00:41
1
user7778181625029
patricia suwerd chanika :
i believe alapken alimoyo and he is somewhere safe but not in this county
2026-07-14 10:48:57
36
tamala301
user4533927536621 :
Soon or later truth will come out. There is God in Heaven, anthu aja ndambiri.
2026-07-14 13:08:04
29
edith95686
Edith@95 :
that means ankafuna amuphe Chilima kunjako Atiii eeeeh afta God fear MCP
2026-07-14 19:11:52
0
stephanfundsonkam
stephanfundsonkam :
Lapukeni man of the moment aaaaa koma if its true kuti you helped kuzimitsa anthu aja God his watching
2026-07-14 14:39:48
1
kaleso.batoni
NKHANYESI ODOKWU ACHINAKA (KB) :
inquiry ikacheze ndi maiwa paseli akapeza zambili
2026-07-14 10:35:11
32
memory0318
Memory :
Ziululika ndithu
2026-07-14 14:27:02
1
agnes.wa.luweya
Agnes wa luweya :
Manda amenewo akuyenela kufukulidwa mwanjila iliyose💔💔💔
2026-07-14 11:31:53
16
user4096554195958
user4096554195958 :
koma kunena chilungamo anthu awa achisilamu amakhala olimba mtima, mwazi saopa kuukhetsa, only God knows the truth
2026-07-14 12:56:09
9
scillahka
🦋scillah🦋 :
Chilipo
2026-07-14 17:11:05
0
aidah.mkwaila
❤️‍🔥Tasha C Beib❤️‍🔥 :
nanga amaziwapo chani akati ndikapita sindikabwelako iii km ngati ndi zinthu nde kuti ndi zinthudi
2026-07-14 10:00:34
12
user73024034611650
vanessa :
Kodi amkanenelanjo kuti akapita ku Korea sakabwela komanso telling the wife kuti azazindikila bwino pasogolo? I feel he knew the whole mission
2026-07-14 15:06:52
8
chisomosilikar
chizmore wa nazombe :
amkadziwapo kathu ndithu
2026-07-14 10:39:54
13
merykazembe559
Mery Kazembe :
ndipo the truth ikupezeka pamandapo😳😳😳😳
2026-07-14 10:46:26
13
user2492814138427
user2492814138427 :
alapikeni amaziwa chilichonse chomwe chimachitika kom sanafune kuwawuza akazawo😭😭azibambo musamatibisile zinthu chonde nanga chilungamo ichi
2026-07-14 12:38:04
6
alicegama099
Aliceh beib😍 :
ambuye pitilizan mavumbuluso anu mpaka chobisikacho chitaululika💔💔
2026-07-14 13:46:23
5
cinto5693
Cinto :
It’s making sense, this woman was saying the truth
2026-07-14 12:21:57
6
sarakimu99
Sarafinaous💋 :
Ambuye chilungamo chioneke tili pa maondo🙏
2026-07-14 11:29:02
7
aarongon606
Aaron :
ndikuona ngat mamuna wake anapanga nao chiwembu kut azao aphedwe chikumbutima chinavuta bamboo
2026-07-14 14:49:47
6
aaron.mkandawire2
Aaron Mkandawire :
aaaa uyuso ndiwa bodza serious
2026-07-14 16:12:43
2
rosechisewu
Rosechisewu :
arapuken akazipo kalikonse serious apa zaziwikilatu zokha mmmmmm
2026-07-14 16:09:31
2
user1130734187631
Faith Feby :
anaziwa kale zakuphedwa kwa anthu bwanji ananyamula passport ndipo osamuuza chilima bwanji eee ndi oipa
2026-07-14 14:42:07
3
stevemphaleidyani
Steve Mphaleidyani :
passport ku ku maliro
2026-07-14 12:41:44
0
brie.last.born
Brie Last Born :
eish 😭😭😭ine ndye zikundikhudza moipa😳😳adzibambo akati abise znthu 🙌😭😭😭
2026-07-14 12:44:45
2
To see more videos from user @manupage09, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About