@e.promise5:

E. Promise
E. Promise
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 15 July 2026 17:08:05 GMT
33860
2750
1138
118

Music

Download

Comments

user8823195061967
scortis :
Ambuye yambilani pa ine udindo wandikulira mwana wanune
2026-07-16 07:22:55
1
immaculate.msosa
Immaculate Msosa :
ine pano mami zichitike ndi moyo wanga
2026-07-16 10:57:26
3
lonelysambuni
Lonely Sambuni :
amen,ndine thandizo la anthu ena koma ndalama yomwe ndimapeza sikwanila ambuye tsegulani makomo a ndalama,zisomo pa ine
2026-07-16 12:41:41
0
millicentditsele1
Mimi :
amen ambuye ayendere nyengo zanga 🙏🙏🙏🙏
2026-07-16 07:06:06
1
beckybabe81
@Beckybbesamson :
ambuye ndikumbukileni nyengo zanga 🙏🙏🙏🙏
2026-07-16 07:34:05
1
frola.j.j.m
frola J J m :
Ameen and amen ambuye ndithandizen 🙏🙏🙏🙏🙏
2026-07-16 07:11:41
1
emily.muthuzi
Emily muthuzi :
Amayi ndi abambo ndibe komaso azikulu anga ndibe so a anasiya Ana komaso ine thandizo rikundisowa kt ndiwathandize mulungu ndithandizen 😭😭
2026-07-15 17:52:03
10
user7455498009839
GraceJames :
ambuye ndikumbukireni Ndine Mutu kubanja kwatu Koma zinthu sizikuyenda
2026-07-16 07:09:20
3
user5824342026336
Mercy elian munthali :
Ameni chisomo chamulungu chigwere pa moyo wanga komaso pa banja langa...
2026-07-16 07:27:43
2
enajas_kitchen
Nachisale the 1st :
Ambuye ndikumbukireni ine mwana wanu
2026-07-16 07:39:30
2
leonardmamu
amina :
Ameen and Ameen ambuye nyengo yanga mukuiziwa ndinu okwanilisa pamoyo wanga Ameen and Ameen
2026-07-16 10:12:20
3
gracieeee169
gracieeee :
Emen and Emen
2026-07-16 01:25:36
1
user8754551205340
Cecilia malanga :
ambuye ndikumbukileni
2026-07-16 07:20:48
1
desmondmaswiti815
Melia Nkhori :
amen 🙏 Ambuye ndikumbukilen ine
2026-07-16 07:27:42
1
user4585139278149
Beatrice :
ndili pano ambuye mwana wanu ndikumbukileni
2026-07-16 07:21:57
1
alli.chirwa
Alli chirwa :
Amena I receive in Jesus name, yehova sinthani nyengo zanga
2026-07-16 07:22:54
1
user8161997382661
Lindah Tuliah :
ambuye yambilani ineyo udindo wandikulira😭😭😭🙌🙌🙌
2026-07-16 07:26:13
1
agnesskambalame96
Agness Kambalame :
Tikumbukileni ambuye,pamene mukudalitsa ena msandipitilire
2026-07-15 18:37:05
2
tendai4887
tendai :
amen mwaona ine pano😭😭😭
2026-07-16 05:55:21
1
malaika.george
Malaika George :
ndilipano mwana wanu ambuye ndikumbukireni
2026-07-16 07:27:33
0
doreen.mafunga7
Doreen Mafunga :
Ambuye ndikumbukireni ine mwana wanu🙏🙏
2026-07-16 09:40:10
0
ratfahmtenjemtenj
Ratfah mtenje Mtenje :
Amen and amen,I eyo ndi modzi amend ndili munyengo imeneyo,ndi chitilen chifundo ambuye ndchitsen manyazi
2026-07-16 05:07:30
1
codykaudan
Cody Kaudan :
amen zichitike ndmoyo wanga pamene chilichose sichikutheka
2026-07-15 18:53:32
1
richard109503
rich @1234 :
Amen
2026-07-16 15:30:02
0
regmollen
Regmollen :
Amen 🙏🙏
2026-07-16 08:53:55
0
To see more videos from user @e.promise5, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About