@zai.teps:

zai Teps
zai Teps
Open In TikTok:
Region: MW
Thursday 16 July 2026 11:27:58 GMT
79080
1881
250
323

Music

Download

Comments

tammialawe
Tammia Lawe :
ine ndi silamu koma izisingakwanise
2026-07-17 07:57:03
16
hajira.mustapher
Hajira Mustapher :
ine mamuna wake wangayu sindingalole mamuna wamabodza ngati mzimayi ndiye mitala sindiye andipha
2026-07-17 14:44:44
14
innocent..............1
Innocent Mphande :
Palibe Mulungu apa kungosata zikhalidwe zaenaake mkumati ndichipembedzo
2026-08-02 06:24:21
0
evelyn.nyadani6
Evelyn nyadani :
koma ndi phuma laineli mitala sindingakhale
2026-07-17 06:21:45
13
mai.mlambo61
Mai mlambo :
Ndi suna mitala ine navomereza
2026-07-19 07:55:13
1
lynna.longwe.27
Lynna Longwe 27 :
ndichifukwa azimai apanonso akumakhala pamitala🤣🤣🤣🤣🤣
2026-07-18 15:45:54
1
pastormzinda
Pastor Mzinda :
misala + ziwanda
2026-07-17 06:34:50
7
emmanuel.josephw
Emmanuel joseph :
ineso kuno tili akazi 2 ndimava kuphweteka koyamba km pano zinazolowela🥰🥰🥰
2026-07-29 14:59:56
0
paps.jones
Paps Jones :
Ndikufuna wa number 7
2026-07-18 20:12:37
0
riamtirah
Aria😎🩶 :
koma anthu inu ndi ankhaza
2026-07-19 08:58:25
0
cathy.matenje
Cathy Matenje :
Moti pamenepo mamuna wanu ndi mmodzi? if yes ndinu opilira Ladies ine singakwanitse 😂🙌
2026-07-19 04:32:09
3
buwa400
buwa :
koma pingo uwu okha inende ai eeeee
2026-07-18 07:49:46
2
estherkachingwe3
Estherkachingwe3 :
😂😂😂Ine nde singapange nawo dzibwanazo
2026-07-19 13:41:16
0
judithnkathama1
judithnkathama1 :
aaa zankutu
2026-07-18 09:46:24
0
user5247781770051
shakira :
zoona kaka munenetche
2026-07-17 21:21:50
0
amizo6757
amizo :
za nice
2026-07-19 13:38:47
0
rite429
Rity :
10-10 pa Mpando ukuuuuu😅😂
2026-07-19 11:53:19
0
eddie73314
Eddie :
where did you get mtima wodekhawo coz mine mmm noo wina akamangilira mwendo mwamba ku central 🧐🧐
2026-07-17 09:04:27
2
getrudsam
getrude :
AI zkm mtima wabwno mlinawo ine singachite ndpo zisazabwere mumoyo wanga dzina layesu
2026-07-17 14:22:39
2
esnart.mtima.kach
Esnart Mtima Kacheto :
ine singapanga mwina nditalodzedwatu
2026-07-18 08:49:23
0
shirabanda28
Shira Banda :
za ziii nchifukwa mpingo uwuu sindisangalala nawo amalimbikitsa zosatheka
2026-07-19 11:11:09
1
user6474789461380nyapi
lucie🌹 :
eeeeeee nditamva nane ndinakapeza mamuna wina....koma siimmene kwavutira....🤣🤣🤣kwathu akuti ndalodzedwa.
2026-07-17 12:22:41
1
shakirachinguwo
Chinguwo Shanta ❤️ :
I'm a Muslim km mitala nde singachite bola nzikhala ndekha iyaaaa
2026-07-18 12:23:01
2
saudah.wa.jawadu5
Saubeib🥀🦋 :
mtima waine ndimangolutsa zilizonse nde sindingapange kuopa kukagona kundende😂😂
2026-07-18 14:55:28
1
To see more videos from user @zai.teps, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About