masha Allah kom chepesana kulankhula mokweza/I mean kut muza ma gwirise ntchto chikweza mawu kupangira kuti mawu anuwo ndifitina kwa anyamata amene ali around
2026-07-17 18:03:06
25
sakina :
mukhale mzanga mamie ndikufuna mzanga olimbikitsana naye za dini
2026-07-18 08:24:02
21
Zayi🥰🥰 :
I admire this woman and in sha Allah I will be like her ♥️
2026-07-18 04:14:04
28
charity :
ndmafuna munthu ondmphuzisa za allah
2026-07-25 12:33:47
2
merv :
ndine Christu koma mwanditengamo saname ,mpaka ndapanga save straight ku status 💗
2026-07-18 17:25:29
9
DENIMO Abdulah :
ndikanakonda ukanakhala mai wantumba mwanga kom kuyambila lelo ndiwe Cictar wang🥰🥰🥰