@manupage09: #malawinewsupdates🇲🇼

MALAWI NEWS UPDATES
MALAWI NEWS UPDATES
Open In TikTok:
Region: ZA
Tuesday 21 July 2026 05:28:27 GMT
52340
2155
331
197

Music

Download

Comments

user693909208823
user693909208823 :
mmmmm pena ndizovuta koma kungot mwana omupeza amavuta kulela ndiochepa omwe amayamika,,mulungu azitithandiza mmmm
2026-07-21 14:35:54
0
miss.kattah
MISS KATTAH❤️👅🇲🇼🇬🇭 :
If you have never been mistreated you won’t understand her Zikomo
2026-07-21 08:41:54
258
its.clarah71
it's clarah :
Amene sanadutsemo mu situation iyi sangandiuze zochita
2026-07-21 08:55:07
54
hagra002
𓏲ּ𝄢 :
uyuyu sanalakwitse kuyankhula nkhaniyi nonse mukuti walakwitsa kubweretsa pa social media ndinu anthu ankhanza muzizukute mumtima
2026-07-21 08:58:52
120
patriciatriciangw
patriciatriciangw :
Mulungu chonde ndisungen ndi moyo wautali kut ndiwalela ndekha Ana anga😭😭
2026-07-21 07:40:37
91
khumbo977
khumbo ❣️ :
amene akuti sakuonapo vuto ndimfiti
2026-07-21 09:50:17
50
colleta59
UNIQUE FASHION WORLD SHOP. :
Inenso ndinene story yanga nda pongozi anga zomwe adandichita 😭😭😭😭😭mtima wanga uphwe,,, big up lopie anthuwa akumaona ngati tinaiwala
2026-07-21 06:44:25
66
nasibeko0
Memory 🌹hun♊️ :
The pain inside her eyes 😭💔
2026-07-21 08:03:44
96
princess.desire87
Princess desire :
komano kumbali yanga sanalakwitse kutengela kwa muthu yemwe wadutsako mavuto ukuyakhula chochi umapepukidwa maiwo mulungu amawasunga ndi moyo mpaka lelo kuti azaone chipambano chanu mama
2026-07-21 06:29:58
42
sbu___
sbu :
very sad ,no child should go through this
2026-07-21 08:25:49
26
ladyporcupine2
Lady Porcupine :
She was built stronger no one can break her !!!!!🥰
2026-07-21 09:39:44
23
philliplast300
Philliplast300 :
za mfilimu ya nigeria, kwangosala ukwatilane ndi Prince kenako a step mother wo azapange regret
2026-07-21 07:51:49
23
sothwayo21
Sothwayo :
childhood trauma ija osazayiphweketsa guys mmmmh
2026-07-21 12:37:59
4
zolalizolia1
Zolah stitches 🧵 :
I think bambo akewo anakhwimila mayake iyaaaa 🥺
2026-07-21 12:04:22
4
arabmoney714
ArabMoney :
Nkhani iyi sinagakhale yopeka.. I believe her and zandikhudza kwambiri 😔
2026-07-21 12:45:06
5
abet.boi
abet boi :
koma amene amat walakwitsa guys mwana wa 7 azuke past 3 aaaa ngat zilizoona ambuye atikhululukire amene tikukhala nd ana amasiye
2026-07-21 07:12:56
24
usersitibeib
Ketilina,Sean na Innocent💓🤳 :
Zikomo Malawi news updates🙏 inetu inandiphonya iyi
2026-07-21 06:51:29
57
tamala301
user4533927536621 :
Odi ndilire kaye ine😭😭😭😭😭😭😭😭🤗Ambiri tadutsamo but we never speak up. May we heal by the Grace of God.
2026-07-21 12:05:03
2
user2955630697165
user2955630697165 :
The pain in her eyes n voice 😭😭😭
2026-07-21 09:32:44
7
fatsanistambuli
Rubbie :
tilipo ambili oti mubwera poyera dziko litha kuzizimuka Bola awo anali a step mum ena ndimakolo eni eni so lopie iweo thanks for the courage it takes courage to speak up anthu asinthe not akwiye Ur teaching the world
2026-07-21 10:43:59
8
bernaphiri
jazzie🥰 :
The pain in her eyes explaining this 💔
2026-07-21 08:59:14
12
ivy2652
Ivykumfunda :
And munthu izi sanganame anthu akuwakambawo Ali moyo never
2026-07-21 08:49:54
18
fazeerachagwa1
FAZEERA JUSSAB :
😭😭😭😭ndendende umasiye ndiwowawa guys
2026-07-21 08:33:52
8
ene0500
ene🥰 :
😅😅😅😅😅 thanks Malawi news ndachoka ku Facebook ku mikozi straight ku page yako ndimve nkhani yonse 😅😅😅😅
2026-07-21 08:06:14
9
marrie3419
🔏 Anabel🇲🇼wa Arsenal🔥🔭 :
zambili ngt zandidusa ndimavela kwa Malawi news 😂😂😂
2026-07-21 05:39:19
11
To see more videos from user @manupage09, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About