@levi.chikwatula7: List yama verse wa muwapeza mu comment section

levi chikwatula phiri
levi chikwatula phiri
Open In TikTok:
Region: MW
Tuesday 21 July 2026 15:14:36 GMT
5841
193
40
43

Music

Download

Comments

user679225885860
EZRA :
Mathews 23: 13 and 14 were combined in other bible version
2026-07-22 09:23:16
0
oli.kaliyaya
oli kaliyaya :
anapita kt ko
2026-07-21 17:47:41
0
thomaskamanga87
love your enemies :
Alo akanacosa mavesi onse inu vutolanu ndi chani?i Ife tanva za chipulumutso from Yesu khristu!kuzera mbible everything is ok
2026-07-22 11:33:06
0
ishmaelmjames
HAUJUI BONGO(NguvuMoja) :
iwe wapeza kut ma verses 😂😂😂
2026-07-22 12:13:11
0
user84206859122724
Restoration :
tifufuze tione then tiankhe bwino
2026-07-22 07:54:42
0
jehunyirenda
Jehu Nyirenda :
Darby bible zilipo zonse
2026-07-22 07:01:05
0
patricktimothy581
patricktimothy581 :
Ndiye muli nazo ntchito yanji? Musapalamule dala mkwiyo wa Mulungu
2026-07-22 10:47:15
0
thomas.chilemba6
Thomas Chilemba :
ndie
2026-07-22 05:08:47
0
samsonbanda302
Samson Banda :
Chilemba chimapha koma mzimu amapasa moyo Yohane 14;26
2026-07-22 09:23:33
0
mphatsodzimbiri
Mphatso Dzimbiri :
pitani mu Chichewa cha malonda mukawapeza
2026-07-22 07:30:10
0
wycklith
wycklith :
aaaa inu bible rake riti
2026-07-22 07:19:17
0
japhetsakala315
[email protected] :
cholinga chanu ndichani
2026-07-22 07:56:07
0
user7296881386113
user7296881386113 :
ine mu bible yanga ma verse awo alimo
2026-07-22 07:09:06
0
vanessamarko249
Shavaxy 💞💞 :
king James version onse alipo achimwene
2026-07-22 06:04:08
0
blessingsmartin2
BLESSINGS MARTIN :
inu mumagwiritsa ntchito ma Bible apanowa.Tamawerengani king james vision u wil find everything
2026-07-22 04:35:30
0
japhet8211
japhet :
Alipo nkhani mkut anaiwala kuika manumber wo!!
2026-07-22 01:16:03
0
nephano.zuze
Nephano Zuze :
zomwe mukunenazo zikusonyeza kuti inu mulibe nzelu. simunaone inuyo powelenga mukhoza kuphophonyetsa Malo moti munene kuti 1,2,3,4,6,7, 9. zimachitika chonncho. ndichifukwa chache ku Bank amawelemga ndalama asanakupatse. koma akamakupatsa amakuwelemgelaso. .
2026-07-22 06:26:54
0
thomsonsant
Thomson Sant :
Kkkkk bro kod umagwilisa ntchito Bible lake litro?? 😂😂😂😂
2026-07-22 09:44:27
0
cassim.thomas
Cassim Thomas :
iweo wadziwa bwanj
2026-07-22 08:38:15
0
madaritso.twahaa
Madaritso Twahaa :
🤣🤣🤣🤣adagawana akilisitu
2026-07-22 07:44:51
0
djvampire4
DJ VAMPIRE, your favourite DJ :
Bible lakolo unachita kutola eeet?
2026-07-22 07:44:46
0
mbewe16
Mbewe jr :
mungaziwe chilungamo anasiyamo zokomera iwo osati mulungu
2026-07-22 07:26:32
0
matheromsatithe
Mathero Msatithe :
sikuti anachotsedwa abwana muchite study mudziwa why they are not found
2026-07-22 09:38:38
0
redeemedpatrickmbayisa
Patrick Nkhoma :
Kapezeni King James version ma verse onse mukuwafuna mukawapeza , ma Bible mukugwiritsa ntchitowo they are copied from that Bible and , nkhani ya kusowa kwa ma verse mu Bible happened ndi ma Roman
2026-07-22 05:47:13
0
levi.chikwatula7
levi chikwatula phiri :
Matthews 17:21,18:11,23:14 Mark 7:16,9:44,9:46,11:26,13:28 John5:4 Acts 8:37,15:34,24:7,28:29 Romans16:24 1John5:7-8
2026-07-21 15:21:50
0
To see more videos from user @levi.chikwatula7, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About