@user8169415761687:

Chirungamo Ndi Bala La Moto🔥
Chirungamo Ndi Bala La Moto🔥
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 22 July 2026 20:17:26 GMT
33931
1464
144
118

Music

Download

Comments

yusuf.d.m
DRIANO MSÀÚKÀ :
M'Chiarabu kugwiritsa ntchito Ife ndi njira yodziwika yosonyeza ukulu ulemu ndi ufumu (plural of majesty) Mfumu kapena wolamulira wamkulu amatha kunena kuti Talamula. ngakhale ali munthu m'modzi izi sizikutanthauza kuti pali anthu ambiri
2026-07-28 22:27:07
0
user56327817361721
¹themba :
amen yes analipod kuyambila pachiyambi
2026-07-29 12:15:48
0
user6296216298455
Jumah Hassan Wasit :
Abusa awa Ali ndi matemberero ndithu
2026-07-24 14:19:47
2
grace.khamisa7
Grace Khamisa :
pa vn ndipati ndiayankhe a sheikh
2026-07-23 12:38:29
4
user6586716800131
jue beib :
mulungu ndiwankulu ssitingamutchule ngat mwana timat ife
2026-07-23 05:29:40
2
jaffalimussah383
Jaffali Mussah :
wamu bible anati tiyeni tilenge munthu. ... pamenepo simunawelenge?? zikusiyana ndimau Oti "Ife"?
2026-07-23 09:38:28
2
pstrichie
Pst Richie :
Mmmm Chisilamu ndichokanika koma
2026-07-23 12:11:49
3
user7621498538150
user7621498538150 :
abusa abodza awa aaa
2026-07-23 09:04:10
3
roberts.alberts
Roberts Albert's :
Ndabalalika ! Kodi chitozo ndichani ? Ndine Mutumbuka
2026-07-23 07:58:30
2
presnelraj1
RAJ 💫 :
Genesis 1:26 is the primary biblical verse commonly debated as an example of the "royal we". In this verse, God says, “Let us make man in our image, after our likeness…”, using plural pronouns for a singular speaker uyu ndbuli ya munthu sakuzwa kanthu kalikose olo a mibawa amuitana fukwa chani
2026-07-23 14:03:29
2
luciusmithekhu539
lucius :
nkhani ndi yakuti ifeyi anali ndindani simpo
2026-07-23 10:36:33
3
charlesnavaganava
Charles navaga Navaga :
zoonadi abishiop mawu owoonadi sheheyo
2026-07-24 15:00:44
1
stellar19.82master
stella💙 :
timati mulungu mulungu mwana ndi nzimu oyela mulungu mwana ndiyesuyo nde muvetse apa nanga simuti anat tipange muthu nde muvetse atakhala kumwamba ndi atate olo mulungu atakhala padziko lapansi pano ndiyesu alimkati mwathu nde nzimu oyera kusonyeza kuti osewa ndi mmodziyo mulunguyo chifukwa inu kuti muyende muli ndi moyo thupi ndi nzimu et zose zili limodzi nchifukwa tili anthu asram mukapsa
2026-07-23 19:12:31
2
user5441240415360
Benson C. :
amen mtumwi
2026-07-23 18:47:38
1
biggysamburton
samburton :
mulungu ndiwankulu
2026-07-23 13:22:55
1
rickcent329
Rick Cent :
Taaazuen a Avala nkanjowo azionera debate a Sheikh Ahmed Detaat azadziwa kt Ife yo amaimilira Majesty osat number ya anthu
2026-07-28 12:53:47
0
user261466249065use
saulosse floriano :
Follow
2026-07-24 15:59:57
1
presnelraj1
RAJ 💫 :
umbuli mpaka kupitana nawo pa radio tu uku
2026-07-23 14:00:54
1
sinositembo15
Sinosi Tembo :
amen
2026-07-24 07:18:51
1
chikolekeneislam
Chikolekene Islam :
Mashallah sheikh mulungu azikudalisan
2026-07-22 20:33:41
2
8sting
Stiñg Moyo :
Kodi program imeneyii imakhala lachingati komaso nthawi zanji?
2026-07-28 18:21:39
0
kelvinbanda968
kelvin Banda :
that's true ineso ndimaikila
2026-07-28 18:44:02
0
user234308632239
M Lee :
next
2026-07-28 15:48:02
1
vow107
Vow Banda :
Jesus Christ is a king of king's
2026-07-28 10:04:35
0
user4043467509102
ellah :
amen pastor
2026-07-28 16:52:27
0
To see more videos from user @user8169415761687, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About