ine mamuna wanga ndiwachisilamu koma anandiuza ndipita ku church kwanga ku SDA ambuye zikomo
2026-07-27 04:37:18
35
Eversmile :
Ambuye ngat wa SDA sapezeka basi banja ine ayi
2026-07-26 19:39:20
28
Sthe🔥❤️ :
Ine nachoka ndekha ku CCAp kupita ku SDA tsoka ndiro eti ndapezaso mamuna wa ku CCAp ndipo ndikumafuna kulira SDA Naiva bwino serious kaya nditani ambuye mamuna osava kuyesetsa Ineso nari kuccap tiyeni tonse ku SDA koma osamva ngati ndizilira nsaname ☺️
2026-07-26 17:21:00
14
HenArmo's handmade bags :
nice🥰.. ine somehow ndimaona ngati anthu amene you leave SDA mumakhala mozunzika/ motsutsika mu mtima until the day you find a 'chance' to return,joy overflows. just a feeling,just a thought,I have never experienced it. but I feel zitandichitikira ndingamve choncho😂.
2026-07-26 21:19:19
15
memo :
ine nalowa Angilican mpaka nabwelera ku mpesa mtima umakana😂
2026-07-26 15:56:35
18
Esther Mzundu :
banja inanditengera ku ccap,kma zikomo ambuye coz zipwilikiti za m'banja zija munazibweresa dala kt ndibwerere ku mpingo kwanga(SDA)mwaufulu
ine amunanga aCCAP,tinangopangitsa ukwati ku CCAP ine kuthawako kubwelela ku SDA🔥🔥🔥🥰
2026-07-28 11:22:24
4
Tio Kaima×2💕 :
Ine mnalowa Anglican chifukwa Cha banja 14 years mmmmmmmm mnabwelelaso ku SDA pano am verrree hapeeeee
2026-07-27 04:51:45
7
Ethel :
si inu nokha,ine pena ngat ndisavale mvano
2026-07-26 16:51:09
8
Tendienavie :
my biggest fear eeh
2026-07-26 20:19:11
3
Mphatso Maonga :
ine ndibwelela ndithu cz ku catholic sindikwanitsa
2026-07-26 18:17:44
4
MEXCO 524 :
just keep praying and ask God to change your situation he is God of restoration Psalms 91, 35, 23 and 102 with faith God hears prayers and he will give your heart desire one day
2026-07-26 18:50:07
1
stella :
zomagovuta ine nabwelera mtima umakana ku CCAp
2026-07-26 13:50:23
5
stellahgomani :
Sumachoka Wense,*
2026-07-26 16:54:17
3
Chaah😜 :
Ndulira,nawe😅
2026-07-26 20:41:43
3
Eddah Mtambo Nkwanju :
ine ndinakulira ku catholic koma simmene ndinkakondela nyimbo za sda ,ithank God kuti anandipatsa mamuna wa mpesa
2026-07-28 15:31:19
4
stellahgomani :
Come back mama,ndipo Mpingo umenewu sumachoka sense ataa
2026-07-26 16:53:52
3
Y🅰NKH⭕ K🅰CHIKW🅰NJE ⓂUSS🅰H :
osangobwelera bwanj??
2026-07-28 13:58:53
1
user4012588260055 :
Tiyeni ku sda inu
2026-07-28 09:17:53
1
Selina Mphoola :
Ife tinabwerera dear
2026-07-26 16:15:41
2
Joaquina :
Ine ndinafika poiwala sabata koma ndabwelera Mu sda
2026-07-26 17:04:27
3
To see more videos from user @user6317447485431, please go to the Tikwm
homepage.