while you are right, not properly explained. Lucious ankasapota UDF pamene zinthu zambiri zinalakwika. on the other hand, Billy Kaunda amatsutsa ulamuliro wa Bakili. Izi ndi zomwe zinapangitsa anthuwa kusiyana komanso kusamvana Kwa nkatikati. Pa nthawiyi nso nkuti Lucious adali mkhala kale mu music pamene Billy was a rising star. Billy anayamba kukondedwa kwambiri kuposa Lucious. izi zinapangitsa Lucious kuyamba tinsanje...
2026-07-27 15:26:54
4
Amier M'bwana :
Active
2026-07-27 08:34:23
1
Ishmael Halod :
inu ndakamuna osadandaula tili nanu limodzi AKUMIZIMU