Macitidwe 3:1 -6 Koma Petro anati, Siliva ndi golidi ndiribe; koma cimene ndiri naco, ici ndikupatsa, M'dzina la Yesu Kristu Mnazarayo, yenda,
2026-07-28 04:23:09
142
OCEE WIGS🇲🇼 :
mami tipangen join prayer team yathu ... we join online it's an international prayer team ....🥰 I can guide you through
2026-07-28 10:55:58
28
agdeatsandtreatsmw :
Not nkhani imeneyo yokha and also uwelengeko *Matthew 9:20–22
* Mark 5:25–34
* Luke 8:43–48
Nkhaniyi imanena za mzimai amene anavutika ndi kutaya magazi kwa zaka 12. Atamva za Yesu, anabwera kumbuyo kwake n’kukhudza mphonje ya chovala chake, akukhulupirira kuti akangokhudza chovalacho achira. Yesu anamuuza kuti Mwana wanga, chikhulupiriro chako chakupulumutsa pita mumtendere.(Marko 5:34)… chonde ukamawelenga usawelenge ndikuwawidwa mtima koma ukhale ndi chikhulupililo
2026-07-28 12:55:33
14
PAUL GAMA :
:Macitidwe 3:1 -6 Koma Petro anati, Siliva ndi golidi ndiribe; koma cimene ndiri naco, ici ndikupatsa, M'dzina la Yesu Kristu Mnazarayo, yenda,
2026-07-28 15:17:19
16
unce stu :
Luka 4:40
Ndipo pakulowa dzuwa anthu onse amene anali nao odwala ndi nthenda za mitundu mitundu, anadza nao kwa iye; ndipo iye anaika manja ace pa munthu ali yense w
2026-07-28 03:46:24
20
Novie 🖤 :
Machitidwe atumwi chapter 3 ...Mulungu akukhudzen ndi dzanja lake la machiritso sis ♥️
2026-07-27 19:47:11
16
Balusungu Nangoma :
Will include you in my prayers. Jeremiah 32 vs 27 more over isaiah 53 vs 5 says it all. You are loved by God dear
2026-07-28 12:54:31
6
Harry budget 🔥 :
Be healed in Jesus name
2026-07-30 07:09:15
0
Yassin Eid :
Yesaya 59 vs 1
Dzanja la Yehova silili lalifupi kuti silingathe kupulumutsa ndipo khutu lake silogotha kut silingathe kumva!
2026-07-28 14:26:20
9
Amina atwabi :
ameen
2026-07-30 05:03:05
0
||𝑭𝒖𝒕𝒖𝒓𝒆||𝑭𝒖𝒕𝒖𝒓𝒆|| :
You r not alone🫵
2026-07-28 20:23:56
0
ASANTE YESU :
Hello Desire
ma Sister in Christ
2026-07-28 11:08:27
0
Rasaac Douglas :
Eksodo 14 vs 14
2026-07-29 06:54:44
0
fredmakula :
acts 3: 1 to 10
2026-07-28 14:59:32
0
DollaGolira🧿 :
Get well soon dear ❤️❤️
2026-07-29 16:53:02
0
GERALD :
it shall be well
2026-07-29 06:03:34
0
Mkandawire Josephine :
machitidwe 3 vs 6
2026-07-29 17:57:28
1
memori :
God is good dear,uzakhala umboni
2026-07-29 14:40:28
0
Wanangwa Gondwe :
John 14 vs 1
2026-07-28 19:16:42
0
To see more videos from user @desireasani261, please go to the Tikwm
homepage.