Natasha zamvere kuno abwerasotu anthu aja akuti waku Dubai ukangodwabwa plane ikupitilira wa Kuwait 🙆🙆🙆😭🥹 ukangofika kukulanda passport abwana okulandira nkukupereka mmanja mwa aluya ukangolowa ku mpanda suzatulukaso mpakana ndalama zomwe anakudulira ticket ndi visa plus ya agent
2026-08-03 17:50:38
0
nelia :
hie
2026-08-02 20:11:35
0
harriet.c1 :
tikudikira mamie tipite nawo kunja basi
2026-07-30 10:32:50
0
Alleeh :
👌👌Mbambande koma cc 🤗🤗tidziwe nawo zambiri timafuna nawo titapita nawo ku Dubai zimakhala bwanji
2026-07-29 20:54:35
0
Gift Singo :
tingodikila passport yathu
2026-07-29 15:33:09
1
Momfelisetgama :
mulicha pati
2026-07-30 08:07:36
0
Theoangie ✨ :
need your number chemwali
2026-07-30 07:23:32
0
Momfelisetgama :
number yayu tipaseni
2026-07-30 08:09:50
0
mervispotan :
ine ndikufuna yokolopa nyumba
2026-08-10 12:47:23
0
juewenga :
Bestiee nde titani kut tikupezeni
2026-07-30 07:53:24
0
alicedaud :
mut titan mwina ndife alendo
2026-07-30 14:39:39
0
Agness13 :
mzuzu tikupezeni kuti
2026-08-01 13:32:08
0
To see more videos from user @dynamfune, please go to the Tikwm
homepage.