maverse omwe alipowa ndiokwana kukalowa ufumu wa Mulungu , ngakhale anachotsa ife tikupita kumwamba basi
2026-08-03 13:34:17
4
quas14 :
After all the Bible is just there for peace on earth. Nothing more
2026-08-03 15:18:16
0
izani :
nkhani ndi yoti tipezereni baibulo losacotsa mavesi koma lachichewa
2026-08-02 11:11:32
2
christone :
ndapanga check ma ves mu buku lopatulika ndipo ndizowona mulibe . ndiye adapita kuti?
2026-08-03 04:26:39
2
ebeneze368 :
i don't buy this argument.
2026-08-03 05:48:34
0
VESSEL OF GOD :
AMen 🙏🙏 Mulungu atitsekule maso
2026-08-05 17:52:18
1
truepaul :
even in king James whole books were removed. the first canon on scripture had 73 books king James has 66. although he translated the other 7 he called them apocrypha. how is it apocrypha if it was in the original bible that was canonized.
2026-08-03 10:01:37
2
Esther Goliath :
nde abwinowo Singapore kuti??
2026-08-02 12:12:00
1
issika :
maveswo nkuva kwanga akuti ma bible ena alipo zinthuzi anachita kumasulila sizingalephele kuphonyeka pena ineyo ndingoti pamene wayimapo usachoke zakazi wambuye coz nthawi yathatu inuyo pezani ma bible akunenawo basi
2026-08-07 15:55:45
1
Shaibu Tembo :
is true
2026-08-02 19:12:38
1
Vinjeru Luhanga :
Interpretation of text is aimed at relaying the exact message and not just word-for-wo. In certain languages, it is impossible to translate say KJV