ineyo chikondi ndilibe nacho mawu ex wanga chibwez chinayamba ndili grade 8 mpaka from 3 pamen natenga mimba yake kuma mwana atabadwa nagonan ndi zanga maliro masten anga ali nyumba ndipoo pomwep napenga mamun ndimadanaye mpaka pano ndipooo mamun ndi galu
2026-08-04 08:34:22
2
Nkhoma lin :
zoonadi tifa nazo
2026-08-11 19:52:49
0
To see more videos from user @dj_kankhwani, please go to the Tikwm
homepage.