@jnw.nyasaland.off: Awa kaya ndindani koma ndiye angomuza chilungamo Chakwera,kuti MCP kuyambila 1994 sichinawinepo chisankho Koma tinawina chifukwa cha bake omwe tinapanga ndiye ngati mufuna kuwina 2030 muyambe mwakonza ma ubale ndi ena aja apo biii muyiwale 2030 Anadandaulanso kuti anali modzi mwa anthu amene anagwila ntchito 2020 koma MCP itangolowa m'boma anyamata amene anawauzungulila a Dr Chakwera anawatsekela chitseko kuti asamakumane nawo Tchaya tchaya #malawipolitics #fyp #fypシ゚viralシ #malawitiktok🇲🇼

JNW Nyasaland Official
JNW Nyasaland Official
Open In TikTok:
Region: GB
Thursday 06 August 2026 22:04:15 GMT
18921
302
81
66

Music

Download

Comments

kennedyponderani1
Kennedy Ponderani :
Utm ndi Mcp?? pompo nditha kutuluka utm pokhapokha ntamuonaso biyeni ndithu
2026-08-07 07:28:22
1
abdulkailu
Abdulkailu :
Mcp ndale mpaka kumaliro eeeeee koma guys imuyo
2026-08-07 06:36:06
1
deviebe990
Michael rob Technician :
Ndine wa UTM koma ndinthokodze this Man kut wandiyakhulira zaku mtima wanga. Dr Chakwera if want to change anything or not take it or leave it but remember Achinachimwendo ndi ena Amakusokonedzani kwambiri thanks🙏🏻🙏🏻
2026-08-07 02:24:52
1
0.brendah
BREKAS :
ndani angadzalore kupanga ubare ndi MCP? mpando mumaufuna koma mumafunaso kupha azanu
2026-08-07 12:05:07
1
memwalssa
memwa :
anthu salora kujoinana ndi mcp kuopa kuphedwa
2026-08-07 11:08:57
1
nkenji1
@nkenji1 :
Kuyankhula km kwachilungamo kopanda mantha🙌🏾🙌🏾🔥🔥
2026-08-07 04:52:35
1
angozo40
Bright Chikondi Loya Kamkwata :
Ndine wa UTM koma ngati ku MCP wayankhula za nzeru ndi uyuyu
2026-08-07 03:24:51
9
user2542523029382
dumi :
I don't think azawinapo anthuawa donia ija inasokoneza mwina chama 2090 mibadyo tilimo itapita
2026-08-07 04:49:38
3
user7381703966231
Shova :
meaning to say ndale zaku Malawi ndizazigawo ndipo sizizasitha
2026-08-06 22:27:19
2
ganizanizuze
Ganieh Zuze :
ine WA UTM nditha kuyikhululukira mcp chifukwa cha chilungamo cha mkulu ameneyu wankhula bwino
2026-08-07 03:04:24
3
user6982216773200
user6982216773200 :
MCP sizawinanso 😂😂😂😂
2026-08-07 03:17:35
5
makondetsa03
makondetsa :
iwalani za 2030 koma MCP mukakanira chakwera nde iwalani zenizeni
2026-08-07 04:08:08
1
aubreymarion7
aubreymarion7 :
Kodi ndikuti uku? koma Pali chilungamotu
2026-08-07 06:22:46
1
nigro978
NIGRO :
Do you know him?
2026-08-07 02:23:04
1
madakatsala
madakatsala :
Mcp kulinthu adyera komanso odzikonda mmmm
2026-08-07 03:26:26
1
mkoko.okafo
Mkoko Okafo💉💊 :
pa maliro nkhan za ndale zikutanipo guys??...aaaah😂
2026-08-07 02:50:11
1
cozytrife
Gareth Ntakwile :
ngati ine wa UTM, ubale ndi inu sudzatheksnso mwina musake kwinako..unless we'll be the one on the ballot
2026-08-07 11:18:54
0
user8208686181661
kiwen Dad 🥰🥰🥰 :
chilungamo chimawawatu🥰🥰🥰🥰
2026-08-07 02:10:57
0
harrymilanzi823
zoe :
ena akuona ngati ai
2026-08-07 07:47:04
0
langtoneaddkted
langtone :
Mau amenewo
2026-08-07 07:17:48
0
peterzakeyu571
Peter Zakeyu :
tha
2026-08-07 12:35:24
0
fatimamarypeters
Fatima Mary Peters :
pamaliro eti mpaka ngati pandale
2026-08-07 12:41:40
0
alfredbysonnamate
Alfred Namate :
walankhula bwinoo... congratulations.. Chakwera amveeeeeeee
2026-08-07 08:32:59
0
bensonhara555
benten :
who is this guy?
2026-08-07 08:37:38
0
kholo870
KhoLo :
kuyankhula
2026-08-07 03:23:20
0
To see more videos from user @jnw.nyasaland.off, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About