@anamandwa: zimene akazi amapanga umawathandiza amai ako 👇👇👇👇👇👇##CapCut #vrial #freefire #viral #fyp

Anamandwa Tv
Anamandwa Tv
Open In TikTok:
Region: ZA
Friday 07 August 2026 18:29:01 GMT
17844
506
22
67

Music

Download

Comments

angelledwerd
Angell :
Zimangovuta koma eeee amuna ambili akumangothandiza kwawo kokha 😭😭😭
2026-08-11 07:54:25
5
jessiekuduya
Jessie Kuduya :
Zoonad akazi ambiri timaiwala kuti nayeso mamunayo kwawo amaiake anamuvutikila kumulera
2026-08-13 05:14:53
3
nyson.samuel.mate8
Nyson Samuel Matebule :
dziko lina azimai oterowo ndi amene achuluka
2026-08-09 09:30:16
0
luwiza.gunde8
Luwiza Gunde :
ndipo zoona zikuchitika koma Zina zimaonjeza
2026-08-08 11:34:01
0
catherine.chiyata4
Catherine Chiyata :
phuzitsani phuzitsani kumeneko
2026-08-12 06:19:45
0
alex.chikapa
Alex Chikapa :
kkkkkkkk mwandikumbutsa kkkkkk takumana nazo izi
2026-08-08 17:43:53
0
user4506907453088
nanana :
kkkkk abambo awa anabwela kkkk
2026-08-08 14:55:33
0
shyreenmasiku
Shyreen Masiku :
kkkkkkk
2026-08-08 06:31:09
1
abdulkailu
Abdulkailu :
Zili kuno
2026-08-07 18:43:28
0
ellen.manjaya
Ellen manjaya :
Kkkkk km
2026-08-08 04:40:17
0
tiyamika.ndawala1
Nadia :
mamuna othandiza mayi ake amandinyasa
2026-08-08 15:59:17
0
user7296136624727
Felix Buleya :
Achuluka agalachawiya kkkkk
2026-08-07 19:35:38
1
user1859878194121
user1859878194121 :
km abambo awa kkk ati rero paine supaona kkkkk pachani?
2026-08-08 07:06:28
1
mackmawunde
IBRAHIM MK :
Koma akulu awa ndimawu a mafazala 😂😂😂o😂
2026-08-12 10:42:41
0
user6988217117560
chrissy :
mamuna osila udindo wamai ake mkazi mmm alikuno
2026-08-08 06:46:06
0
mamademama89
Mwai Njunga ❤️ :
osamva ndi osamva... waulemu ngwaulemu sangayambe ulemu chifukwa mwamulangiza 2 days
2026-08-09 08:37:18
0
jessiemwalemwale
PEACE OF MIND HJMM🫶 :
ndipo zoona akuchimuna kuchita kuopa kubwela pakhomo lamwana wao mmm
2026-08-13 11:39:11
0
yotamu718
[email protected] :
palibe zokwatiradi koma bola kachasuyi
2026-08-17 16:32:09
0
user2781336519783
♥️♥️♥️ :
😅😂😂😂
2026-08-10 03:55:47
0
jessie.kayange7
Jessie Kayange :
🤣🤣🤣🤣🤣
2026-08-21 11:04:42
0
To see more videos from user @anamandwa, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About