@tauraimacheyvonne: @Beegee @Mr Free😎

🤎Taurai Mache Yvonne🤎
🤎Taurai Mache Yvonne🤎
Open In TikTok:
Region: MW
Saturday 08 August 2026 18:30:35 GMT
95354
5555
650
302

Music

Download

Comments

christinasabwera
Christina Sabwera :
Kkkkkkk Ndiposo,,, timakaika madzi ku bafa kuti akasambe ife tikugwira gwira mu wallet 😂😂😂😂
2026-08-09 14:32:49
0
effajames
Effa James :
Muuze mwina sakuziwa kut wallet ndyifunika
2026-08-09 08:20:36
1
mawindo83
mawindo83 :
kkkkk koma wamuchita bwino
2026-08-09 08:45:26
3
ester48551
Ester :
Send him back 😂😂😂🔥🔥🔥🔥🔥
2026-08-09 06:43:29
1
sbchinji8
Sbchinji :
A thinker. Lesson to a lot of people. People can't even call your name but come up with lots of demands
2026-08-09 08:26:27
1
zww.891256
. :
Uyuyu ndi mkazi wa zonse momo
2026-08-08 22:21:15
21
beatrice.dzuunde
Beatrice Dzuunde :
2026-08-09 19:26:18
2
memory.chimaliro5
Memory Chimaliro Evangelist :
Am sure..I.will do this...someday😂😂😅😅
2026-08-08 19:28:58
2
tituschipokosa865
Titus Chipokosa :
ndinadziwat kt ma comment adzadza ndimahule
2026-08-09 08:08:09
4
mirriambandah785
Mirriam Bandah :
ndikuwonela muma 23 32 yawutsiku ndaseka ngati anthu sanagone kuti ndimasana🤣🤣🤣🤣
2026-08-08 21:33:25
3
christopherjuliu20
Christopher Julius :
😂😂😂 koma azibambo tiyaluka
2026-08-08 18:48:11
6
marister2019
MARISTER :
wandiimilira Tau akuti ATM andibera limodzi ndi ID woti ndalama zivuta kukatululutsa ku bank 😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
2026-08-09 07:51:00
2
call.her.nancy
Vimbie waelton wemukwekwe 🥰 :
hec ndonzi vimbie musikana waelton wemukwekwe
2026-08-09 12:45:21
2
rhodacaptain
Rhoda Captain :
Ndili pa mbuyo pako Tau!!!! 🥰🥰🥰🥰 inenso sindikwanitsa
2026-08-09 04:54:43
3
user9597220zuluwoman
carlo zulu woman🇲🇼🇿🇦🇿🇲 :
@🤣🤣🤣🤣🤣🤣aiwala bwanji wallet Kwa akupita Kwa mkazi aaaa
2026-08-08 19:31:09
2
user4699757195373
Ebenezer mwendera :
kkkkk achina ndaiwala wallet kkk
2026-08-08 20:03:55
1
anitel1607
anitel_gondwe :
Wakabaza wakondwatu Ali mma win😂😂😂
2026-08-08 18:55:30
4
mariam.chambo1
Abiti Chambo :
ayooooooooooo🤣😂🤣😂🤣😂🤣😂🤣muli ndi mau begee?🤣🤣
2026-08-08 21:04:03
1
kennethnankhwema6
wiwe😍🥰 :
ɪᴄʜɪᴄʜɪ ɴᴄʜɪʟᴜɴɢᴀᴍᴏ ᴛᴀᴜʟᴀɪ🤣🤣
2026-08-08 20:11:09
2
user12793676521905
Christina billy :
Ali pa geez amakhalidwe otelewa, chemwali ndimagwira chipatalamu koma card yanga yabloker ndiye tpt ndilibe mungakhaleko ndi 2pn
2026-08-09 09:23:22
1
achejoe06
Ma Needs 🎲 :
wallet Kodi ndi chani mwati? 🤣🤣🤣 chikuoneka kuti ndichofunikira kwambiri
2026-08-08 19:24:56
2
alice.lihoma
Alice lihoma :
koma kumeneko
2026-08-10 08:01:32
0
fridaynamaona
Friday namaonafriday946@gmail. :
game inatembenuka mesa
2026-08-10 08:10:42
0
manjiri82
Manjiri :
hahahahaha
2026-08-10 08:21:11
0
To see more videos from user @tauraimacheyvonne, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About