@woft.online.churc: Eeeish our Chair tasweka Rest in peace our chairman of the board of elders Pastor Brian Banda 😭😭😭😭😭😭

WOFT Online churchWord of Fai
WOFT Online churchWord of Fai
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 09 August 2026 19:27:53 GMT
53770
1700
81
62

Music

Download

Comments

user5161494984218
Bless J :
Anthu ake a Mulungu amapita amoyo kumwamba 🥰🥰🥰
2026-08-10 07:55:09
1
user9762679935312
so :
Dziko lapansi palibe mtendere ndithu
2026-08-10 08:54:59
0
jadedia21
@JADEDIAH21 :
Koma Brian wandiwonongera 3 days yangai😭
2026-08-10 04:27:55
6
procha66
Procha :
koma ambuye inu mwaloladi kuti tidzipita mwanchoncho
2026-08-10 05:58:10
1
nyamithi1
Jane :
infa yowawa yokhuza abale inu aaaa
2026-08-10 04:55:36
2
elliannarinnah
Mekadesh :
I can't believe it.... koma paja muzonse tiyamike Ambuye
2026-08-10 05:02:09
1
tricia.kay11
🌺Stella's Mum..💥 back up :
imfa yaanthu Ake imkondweretsa zikomo ambuye pomuthawitsa uyu kuzolemetsa zadziko lapasi🙏🙏🙏
2026-08-10 04:30:50
18
user267219139313
user267219139313 :
Munthu uyu sanali munthu wamba,kumwamba kulemekezeke.
2026-08-09 22:29:14
26
enelesschisokeza
queen ene82 :
😭😭😭😭😭😭aaaaaaa koma abale ngati angomubwenzatu kumwambako
2026-08-10 03:04:56
3
user8072103360652
Nya Kaunda :
Munthu yu amakonda Ambuye...... Mulandiren mwana wanu Baba😭😭😭😭
2026-08-10 05:10:27
4
tateman54
TATEMAN :
moyo wathuwu ulibe phindu koma yehova yekha
2026-08-10 04:25:48
2
nthanda00
Nthanda :
Wapita wa gwaaa Brian. I still can't come to terms with it 😭😭😭😭😭
2026-08-10 04:52:24
5
fatima.banda83
Fatima Banda :
koma ichichi guys chapweteka gulu eish😭😭😭😭😭
2026-08-09 20:36:01
5
user9153002609435
stofra2528 :
MHSRIP mulungu Amakhala ndi dongosolo lake . ntchito yanu Ambuye yo mwe Muna mupatsa ndiku khulupilila wa maliza . ife ngati adziko la pasi tikuti mzimu wake uziusa mutendele . MHSRIP.
2026-08-10 03:41:10
2
chimwemwematiyasi
Joseph :
mulungu salakwitsa uyu anali thumiki wake sanafune adwale pofika potaya chikhulupiliro pamulungoyo
2026-08-10 03:58:58
1
user114092723161
Jordan :
eeeee God is so wonderful
2026-08-09 20:34:26
1
user0990374319
Tiwo mk😍 :
obanda lero kulibe akuyenda chogona koma moyowu eshiii😭😭😭😭😭
2026-08-09 20:15:54
1
user6665829159975
user6665829159975 :
mmmmmhhhhmmm am speechless
2026-08-09 21:11:55
0
user6085531103484
Francisco :
Pepani church mwaluza chiphona
2026-08-10 10:26:56
0
chrissy.chigwenemb
chrissy chigwenembe :
koma 😭😭😭😭😭
2026-08-10 10:49:39
0
naphychimpanzi
Naphy :
Rip
2026-08-10 09:52:02
0
ma.juh22
Ma Juh😍 :
abwino sakhalitsadi kd? Yesu munatii mnchilichose tikuyamikeni, dzina Lanu lilemekezeke.
2026-08-10 09:37:17
0
kokoanony
koko :
Aww Brian 🥺
2026-08-10 10:22:15
0
tamenjimbamb
tamenjimbambo :
Aaaaa mwawanthu 😭😭
2026-08-10 08:57:16
0
mkbandanda
STAR SHIP TROOPER :
R.I.P
2026-08-10 00:34:17
0
To see more videos from user @woft.online.churc, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About