@martin.mcky: Replying to @starthebosslady2

Martin Mcky
Martin Mcky
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 09 August 2026 20:56:09 GMT
75274
2740
185
313

Music

Download

Comments

patriciamasamba28
Patricia Masamba :
titachita pepper Sunday machurch onse akatolika sizingatheke
2026-09-02 10:02:07
2
mariachinseu
Maria Chinseu :
mwachikondi zitha kutheka ,tilipo ambiri
2026-09-02 12:12:47
0
user7384958155768
user7384958155768 :
zoonadi
2026-09-03 11:58:36
0
marriamhussein851
HusseinMarriam :
Even oti si akotolika titha kusokha nawo nyimbo za Paul Banda zimandisangalatsa 🙏🙏🙏
2026-08-10 08:25:10
10
kingchiccotwice
Chicco twice :
ma church onse in malawi atangopanga dedicate chopereka cha Sunday limodzi ikhoza kukwana koma afiti onamizila kupephela inu simungapangeyi
2026-08-10 14:13:10
6
matthewsaddam
Matthew’s :
Zoonadi😭😭since Lucius chimwalileni akusowa mtengo ogwila
2026-08-10 15:30:08
3
wazilhakim69
wazil :
Ine ndi msilam koma ndata kusonganawo,,,
2026-08-27 13:04:22
1
memory.996
Memory🌸 :
koma ndiyedi.. Mulungu akudalitseni Mr Paul Banda
2026-08-31 10:59:43
1
fabianobenni
fabianoben3 :
zoonadi tiyeni timuthandize munthuyu
2026-08-10 12:46:09
1
bensongerevazio
Benson :
Please ndi ngalumikiza ne bwanji ndi sir Paul banda
2026-08-11 07:10:32
0
chiwato.vin
Chiwato Vin :
inenso nditha kusonkha nawo koma please
2026-08-15 15:56:10
1
yohane.nyasulu
Yohane Nyasulu :
ine siwakatolika koma ndimamukonda Paul Banda tiri okozeka kusonkha
2026-08-23 16:00:15
0
briekays1
Briekays :
anthu awa they were so talented bwanji, 😭 lets help paul abale
2026-08-15 21:23:15
1
daviedick6
Davie Dick :
inenso mundiike nawo mu program
2026-08-13 17:18:07
0
sellinachauma
Sellina chaumasellina60@gmail. :
ine ndimadabwa ma church ambili amakonda munthu pamene alibwino Ali ndalama ,koma munthuuja zikamuvuta ,matenda,ndi zina zotero mpingo suchitapokanth
2026-08-23 07:39:10
0
jamesali558
James Ali shamilu :
ndipo live let's help him
2026-08-23 16:21:25
0
mike51333
MIKE :
ineyo sinkatolika Koma program imeneyo ndaikonda zed
2026-08-10 15:13:25
0
mikeosman700
Mike Osman :
sir Paul banda akudalitseni mulungu
2026-08-10 15:15:53
0
user9020184676799
Eng.Francis :
not only Catholics,as Malawians,let's do something
2026-08-14 16:20:00
0
dalitso146
Dalitso :
Koma nfundoyi yandikhudza, titateno ambuye azatidalitsa ndithu
2026-08-13 16:52:40
0
user9837281678581
Chiwondo :
Ma comment sangathandize,bwanji tiyambepo guys
2026-08-13 02:59:27
0
bernadette.sanaze
Bernadette Sanaze :
Zoonadi izi tichitepo kanthu
2026-08-21 07:29:03
0
user9795299668723
AUB MH :
Not only a katolika koma amalawi tonse munthuyu watisangalasa kwa nthawi ya itali ..... aliyense kupeleka k1000 anthu 20 million ndi ndalama zingati?
2026-09-01 12:12:43
2
asyasyeajaluche27
Asyasye ajaluche traditional d :
zimandikuza ine ndikamawona Paul banda choncho or radio 📻 maria osapanga kanthu eish tipatseni account ndiwona mmene ndingaperekeyo
2026-08-11 02:15:50
2
waynedepatrao2
Wayne de Patrao :
koma tiyeni tichitepo kathu kusatengela chipembezo nyimbo za Poul Banda zimatditsimutsa kwambri
2026-08-10 09:51:36
2
To see more videos from user @martin.mcky, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About