Language
English
عربي
Tiếng Việt
русский
français
español
日本語
한글
Deutsch
हिन्दी
简体中文
繁體中文
API
Home
How To Use
Language
English
عربي
Tiếng Việt
русский
français
español
日本語
한글
Deutsch
हिन्दी
简体中文
繁體中文
Home
Detail
@rafickbyson58: #RIP Brian Banda#
JAY COMICS
Open In TikTok:
Region: MW
Monday 10 August 2026 10:39:13 GMT
78857
2080
231
166
Music
Download
No Watermark .mp4 (
0.5MB
)
No Watermark(HD) .mp4 (
0.54MB
)
Watermark .mp4 (
0.95MB
)
Music .mp3
Comments
Katunga :
Abwino sakhalitsa koma achabe anakhalitsa kuti mwina angalape
2026-08-12 04:34:54
1
widzmax (mr night) :
maplan amulungu si amunthu dala, omwe timawafunira zoipa amakhalitsa ndi moyo
2026-08-11 05:52:40
1
reginamatatiyo :
Ndipotu wafa ndithu mkutani? Chakwera ndimunthu waMulungu mukhaula
2026-08-11 08:30:11
1
Rhoda Richman :
kulakwisa kwambili anthu mumaganiza bwanji munthu mumudelanji kodi kulakwisakumeneko mulungu akuchitile chisoni wava
2026-08-10 20:25:33
3
munez 7 :
iweyo uzamusiya chakwela akadali moyo that guy is loved by God ase
2026-08-11 11:48:38
3
Maria musaiwa :
chakwelaso naye ndimuthu adakulakwilani chani abale ifa idalembedwa kuti tonse tidzafa tidzangosiyana manyamukidwe basi tiyeni tizifunilana zabwino amalawi mmmmmm ai
2026-08-10 20:42:18
4
YAMIKO :
munthu pampando munamchosa ndiye chomdera ndi chani? mulungu akuyendeleni mwapadera
2026-08-10 17:49:10
29
Chancy Mandah :
Chomwe ndimadziwa ine ntengo wosabal sulasidwa kom wobala ndie umagendedwa chakwel ndintengo wobala mugendeni tcholani ndithu zipatsoz
2026-08-11 04:32:23
12
Banda Frone :
Kuteroko mawa umwalira ndiweyo uyoyo Mulungu anampatsa moyo wautali.
2026-08-11 08:21:15
8
ambrose Stanley Sumaili :
Nde mwaonatu zomwe amapanga mulungu osamalimbana ndi amene mulungu anamupatulla
2026-08-10 19:38:50
7
jenifer msiska :
Abale tiyeni timuziwe Yesu,tisazipalile moto,pepan ngat ndalakwa
2026-08-11 07:17:09
6
TKFIRST 01 :
wakufa sadziwika nchifukwa chake mulungu anatibisira liopeni mawa
2026-08-10 18:17:15
10
staff boy🇱🇾🇱🇾 :
kuyakhula kopusa kumeneko mulungu siwopusa ay pezani Zina zo posta please 🥺🥺
2026-08-10 17:40:02
9
tadziwabango :
mchifukwa chake Mulungu watenga amene mumufuna mkusiya amene simumufuna kumayankhula bwino
2026-08-11 05:03:31
4
ciarabanda :
aaaaaa mwaganiza bwanji achimwene aliyense moyo amaufuna km kumwalila sachita kusakha
2026-08-10 19:35:01
7
Sakina kandulu :
mulungu amatenga yemwe wamukonda
2026-08-11 03:42:26
3
groly :
mungochimwapo inu mulungu salakwitsa, muzingoyamika mulungu kuti inuyo muli moyo.
2026-08-10 22:54:07
3
Gladys Goliath :
ma plan athu sali ma plan a Mulungu
2026-08-11 04:00:29
3
betadayz ✅️ :
nizoona wawa
2026-08-10 18:33:50
3
Sarah nyakhumbo :
ayi zimenezo siyani
2026-08-10 17:37:21
4
abet boi :
nae nthawi yake yakwana aliense alindinthawi nae yake ikubwera guys don't do that
2026-08-10 20:03:20
4
user5487203070513 :
ndipo wafatu mufuna azanu amwalire wakulakwira chani mulungu akukhululukireni
2026-08-11 04:25:33
3
saidi :
aaaa kusowa zochita
2026-08-10 17:18:25
4
Joseph Banda :
ndipo zoonad
2026-08-10 16:31:53
0
Jennifer Chimzumanzi :
aaaaaa murini vuto
2026-08-10 18:28:23
3
To see more videos from user @rafickbyson58, please go to the Tikwm homepage.
Other Videos
sunscreen foundation yg lagi viral nih #carslan #carslanid #carslanfoundation #carslan2in1sunscreenfoundation #foundation @Carslan ID
The peak of Evolution.. (New Trend?) SONG MONTAGEM HYSTERIA - @preymsc @pvppet @ToufG (gladeoac) @HXI #rezero #subaru #mangaedit #anime #edit
#війнатриває #specialforces #хочуврек #війнавукраїні #врек
Replying to @🍒 2016 inspired for Eid or Prom 💫🖤✨ @patmcgrathreal foundation @tartecosmetics shape tape @patricktabeauty she’s sculpted @simihazebeauty red moon @patricktabeauty major dimensions @morphebrushes rich & foiled gold seeker (use with setting spray) @makeupbymario quartz (applied on top bc it adds sparkles ✨✨) @anastasiabeverlyhills lash sculpt @houseoflashes divine lite @shiseido white eyeliner (the easiest to apply that I’ve tried so far - I wasn’t fighting for my life lol) @hudabeauty cherry blossom powder @hudabeauty pinky brown liner @hudabeauty honey gloss (SO GLOSSSSYYY the video doesn’t do it justice) @charlottetilbury setting spray (I use a lot for dewy finish bc my face is dry) #eyeshadow #eyeshadowtutorial #2016eyeshadow #2016makeup #makeuptutorial #makeupoftheday #smokeymakeup #eidmakeup #prommakeup #goldeyeshadow #makeuplook #smokeyeyelook #fairymakeup #makeupideas #eyemakeupideas #glammakeup
affordable lang #tissue #facialtissue #rorosofttissue #affordabletissue #hangingtissue
Portions of Southeastern Indiana, northern Kentucky, and far Southwestern Ohio are in this warning. Cities in this warning include Harrison, Bright, and Hidden Valley in Indiana.
About
Robot
API
Legal
Privacy Policy