@eliza_james_:

Eliza James🥰🎤❣️😋
Eliza James🥰🎤❣️😋
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 16 August 2026 08:28:47 GMT
240289
10105
1023
710

Music

Download

Comments

user2972459816552
Grace Msiska :
mulungu akupaseni chosowa chanu
2026-10-10 15:27:27
0
user5457067934545
RUTH JU :
ndikupatsan ot ubereke my dear oneso ndadutsamo
2026-10-10 22:56:14
1
grace.nangantani
grace nangantani :
eeee ayi ayise ukuwoneka kuti utha kulalikilatu dear ambuye ambuye akupase chosowa chako🥰
2026-10-10 19:33:52
2
user1800701870861
Gradys mbizi 🥰 :
koma mutatumikira mungararike sister muri ndi mphaso
2026-10-09 12:03:03
1
user43184614752122
Brenda nyaude :
uli ndi mau ngat mtumiki wa mulungu
2026-08-16 15:33:46
290
kettie.baulen
kettie baulen ❤️ :
obisa tchimolake sazaona mwai Mulungu akudalitsen mami
2026-10-09 11:22:59
1
womanking897
Mâmåçîtã🌹❤️‍🩹 :
Chifukwa Cha video iyi, mulungu akuchitila chokoma 🫂
2026-08-16 21:20:41
129
febbemara
febbe :
voice imeneyo olo chiwanda sichingaimepo voice ya utumiki iyi
2026-08-16 17:31:09
108
glorifiedpattie
Machau :
tsegulani ministry Mai ine ndidzakhala wa praise team
2026-08-16 19:39:34
44
stella.phiri.gosp
Stella phiri gospel singer :
iweyo ukhala olalikila ndithu mulungu anakudalitsa ndi mawu ngati ntumiki ingolandila yesu bas
2026-08-17 07:17:47
64
thegrace960
thegrace960 :
You have a very good pastoral,grounded voice may God use you
2026-08-16 16:48:39
22
user1256867496680
Elizabeth :
kuyankhula kokha wayankhulako walapa machimo ako ndiodla muthu yemwe sabisa machimo ake mulungu akuyendere mama nkukudalitsa uzamupeza mwna komaso uzakhala olalikira mudzina layesu🙏🙏🙏ndakupanga follow wandisangalatsa
2026-08-17 11:20:52
31
charity.kamundi
[email protected] :
Tikanena kuti tilibe uchimo ndipo tikudzinyenga tokha,. wobisa machimo ake sadzakhululukidwa iweyo Mulungu akuyendere ndipo akwanilitse chokhumba Cha mtima wako🙏
2026-08-17 17:52:16
36
wajamucarol
wajamucarol :
mulungu amakonda okhawo oyakhula chilungamo ambuye akukumbukireni mandilimbikitsa saname ndaphuzira chinachake saname
2026-08-16 17:07:29
29
kamanbpsgnv
Natasha :
Akunama osakhala ntumiki. Just focus on yourself and trust God. It is well
2026-08-20 08:56:06
27
user1475274653374
user1475274653374 :
mulungu akupase chokhumba chako mamie tsiku ngati larelo uzakhala wayamula mwana wako 🙏🙏🙏🙏
2026-08-19 02:11:33
5
abigail.kapichira
Abigail kapichira Banda❤️♥️ :
Ndipangen like ndigule bundle 😩
2026-08-16 19:07:28
50
user94108570602206
fatie :
I just love ur voice I don't know why?🙌
2026-08-17 05:17:58
6
jaynechapombagemstones
Jayne Jaydacris Chapomba :
beautiful voice honey
2026-08-24 16:15:34
6
mercie2491
Mercie🥰 :
ndipangen like ndionelele nthaw ina
2026-08-20 19:29:54
5
tishotisho1
Tisho1🌸❤️ :
What a story 💔🥹 it shall be well hane.
2026-08-17 07:16:19
6
user14921923297045
user14921923297045 :
Zizatheka ccc mulungu sachedwa ndipo alipo
2026-08-16 17:59:46
6
hildaannie2
Hilda❤️ :
I quote" ineyo nali hule"
2026-08-18 14:32:29
9
useresnarth3803252068844
Miss Nabandah❤️ :
mulungu ndiwadongosolo,sachedwa safulumila
2026-08-16 15:14:44
12
madalitsomatengo
madalitsomatengo :
ntendele wamuntima uja ndiofunika ndipo mweiwe muli chilungamo chokhachokha wandiaangalasa
2026-08-18 16:52:59
5
To see more videos from user @eliza_james_, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About