zonsezo tikupanga km ngt iye sakukupangira zabwino titani?
2026-08-19 07:24:40
0
user7062373740951 :
Ine latha miyezi 5 yapitayo nkhani Ulemu panalibe,mwakani,kutchalenjana,nkhani zama rights nkatimo,nanji mkazi akangoyelekeza kuti akugwira ntchito kapena akupeza ndalama through business they dont value banja ndi mamuna.
Another biggest problem imene mabanja sakukhalitsa masi ano is Social Media.WhatsApp,Tiktok ndi Facebook azimayi ambiri akudederuka nazo.
Akumanamizidwa mosavuta ndi anyamata ndi azibambo odyera pakamwa.
Mapeto ake ma regret.
2026-08-19 06:32:31
0
Frackson Binuli :
on point 👏👏👏
2026-08-19 08:00:08
0
Lamson Namukhonde :
😂😂😂 zoona masten 😂😂
2026-08-17 03:09:52
0
To see more videos from user @yoemajor2, please go to the Tikwm
homepage.