@iamchamasowa6: #onthisday

CHAMA🍒EMPIRE🍒 🇲🇼
CHAMA🍒EMPIRE🍒 🇲🇼
Open In TikTok:
Region: ZA
Wednesday 19 August 2026 15:09:15 GMT
156002
4130
206
735

Music

Download

Comments

salomymakoza
The blessed one :
chidule kugula ndikupempherela usanayambe kugwiritsana ntchito .luke 10 vs 19 God has given us power to trample over satan and the power of dark ess
2026-08-20 09:26:48
53
reen647
reen❤️ :
mbali zakwanuko zimenezo! aaa
2026-08-20 08:55:09
43
cutekissah03
kissah👣👣 :
zopusa bas wina asandipangeso like ine
2026-08-21 19:53:47
6
user514318570656
@geramom :
atsikana tizimvesesa ndife amwano heavy et life, tiziwona
2026-08-20 07:07:57
6
moureen975
moureen975 :
inu anthu mulungu amatikonda akanakhala kuti amalola kuti anyani amenewo mulungu amalola ziphavuzawo ziziposa phavuyake bwez titathakale, muzikhulupilila mulungu basi
2026-08-21 09:33:25
2
enelessmainja
Eneless Mainja :
Mmmm ambuye atithandize pa tokha sitingathe
2026-08-20 10:44:08
5
roxnixx
Rozz Nix :
Ndipo zameshizo ndava kambili mbili eeee ndimat ndiyambe kumanga kma pompano ndikukameta
2026-08-20 08:06:20
5
walinacy4
Walinacy :
bible limanena kut...zokhumudwitsa kapena kut zoopsa sizilephera kudza pa moyo wa munthu .. koma tsoka Ligwera kwa iye amene aadza nazo
2026-08-21 06:51:56
7
emmah572
nafetebu :
Kkkk esh nde tizivala chani esh
2026-08-20 11:27:23
1
meimoey6
🍫 dark mei ❤️🤎 :
chilichonse ndichasataniki
2026-08-21 08:33:57
0
ww.mwachandelinnie.com
Linnie mwachande :
God is good u'll no one is greater than God
2026-08-21 05:51:39
6
blessching0
Blessching :
Zaziiiiiiii ukoooooo
2026-08-25 20:01:09
1
ngozo.jozy.matoli
ngozo Jozy Matolino :
nkhondo zathu ambuye mutimenyele
2026-08-20 18:13:58
3
phiriezelet
phiri ezelet :
Ambuye kodi mwagona mbuye wanga😭
2026-08-20 10:45:46
6
user6138808411375
Tamanda :
Ai fenks
2026-08-20 14:00:58
0
gracian543
gracian :
koma ziliko
2026-08-20 13:52:29
2
user91816694970153
Rabia peterson :
Zosayenda
2026-08-21 12:49:09
1
kampiranafe
Nafe :
Ambuye atitetezele
2026-08-20 05:23:20
5
user982254738
Rechoal :
patokha sitingathe km Ambuye ndinu oteteza ,sizomse zomwe tingaziwe kt sizabwino km chifukwa cha inu Ambuye tipambana 🙏🙏🙏🙏
2026-08-20 07:41:34
5
user8176869990475
patrick arsenal chikomeni chiz :
ineyo ukuku ndimapitako
2026-08-21 16:17:44
1
olivia.zimba0
Oli coringz :
mulungu timenyeleni khondo patokha sitikwanisa
2026-08-21 17:23:28
1
aishakamoto215
mum's last born 🇲🇼 🇿🇦🥰 :
ndye mwakamba late tu 😂😂😂
2026-08-20 12:45:11
2
peturoraudeni
Young malawi ob :
Follow
2026-08-20 19:13:50
1
shakilamalanga
shakira Malawi🇲🇼🇲🇼♥️ :
ai fenkis no school too much money 🙏🙏
2026-08-21 10:02:04
1
To see more videos from user @iamchamasowa6, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About