@kaybeste: #Gospel #worship#fyp #praise #christianity

BESTER
BESTER
Open In TikTok:
Region: MW
Wednesday 19 August 2026 19:28:59 GMT
111917
8078
1449
1453

Music

Download

Comments

graygrace114
user2027355459565 :
sikuchepa zaka ai ambuye ochimwa ndiine moyo wanga simupindula nawo monga mufunila🙏🙏
2026-08-20 06:46:13
6
chim2955
Chim🍓 :
Amen mama🙏🏽powerful
2026-08-20 06:08:11
2
felister984
Felister :
ndakhala ndikumva anthu za Mai awa koma lero gululu kumwamba kulandile ulemu ndi matamando
2026-08-20 05:59:02
6
kaposka5
kaposka :
muzitigawila ulaliki wawo
2026-08-20 09:04:17
3
aubreyjohn35
Aubrey John :
ine mtima ofuna kuthandiza makolo ndimakhala nawo koma vuto ndimapezedwe anga
2026-08-20 06:53:36
52
user6803301478431
user6803301478431 :
amen and amen 🙏
2026-08-20 05:29:10
2
pempho062
pempho :
ambuye ndikhululukreni ndine ochimwa ine 😭
2026-08-20 06:20:19
31
tiyanjanethomas
tiyanjane thomas :
mpaka ndalila ine ambuye chiyani nd moyo wanga
2026-08-20 06:41:35
7
mkaziwaarsenal7
Mkazi Wa Arsenal7 :
19/08/2026 kuona mayanga akutsazika 😭😭😭😭😭moyo wanga wasweka
2026-08-20 06:26:03
19
onachibwe
Onachibwe :
Mulungu imvani pempero langa kut ndipeze mwayi wa ntchito ziwathandiza mayanga ndimafuna mayanga azisangalala
2026-08-20 07:42:18
10
bubblylebo1
mummy Michelle ❤️ :
ine mtima ofuna kuthandiza nde ndilinawo koma ndilibe chili chose olo ntchito sikupezeka😭😭 ndalama kupeza kovutaa
2026-08-20 08:45:55
7
user5161494984218
Bless J :
Powerful preaching🥰🥰🥰 First time kumvera uthenga wa amayi awa, koma muli mphatso ya mtengo wa patali. Kulalikira ngakhale za beat ya zida zanyimbo. akuti nyimbo ya ulesi 😳😳 Ndigaileni video chonde.🙏🙏🙏
2026-08-20 05:29:38
18
dowadonzo
doricabandawe :
abale pangan zot tipange save😭😭😭😭😭
2026-08-20 06:16:46
10
hendersonchaonong
Henderson Chaonongera :
Mayi Madzi atayika,Adabwerako kwathu ku 50, Chikungu CCAP🙏🙏
2026-08-20 07:16:52
5
dimariabenardnsam
Di mariah :
amen
2026-08-20 04:39:06
2
lilliannewa
Lillian Newa :
amen and amen 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
2026-08-20 04:54:48
1
ellah.zulu
mama Jane, Samuel & Groly :
Amen 🙌
2026-08-20 05:25:51
2
user32048472670941
user32048472670941 :
amen
2026-08-20 04:23:36
2
rabeccangoma710
Rabecca Ngoma :
Amen
2026-08-20 07:23:03
2
.onious.queen.bab
# ONIOUS Phiri :
Amen
2026-08-20 04:28:48
2
user67423748823280
[email protected] :
amen 😊
2026-08-20 04:27:39
2
user3424082526671
Alice Banda :
Amen 🙏
2026-08-20 06:16:03
2
gracebeib24
Grace bae😘💕 :
Amen 🙏
2026-08-20 06:20:01
2
user974974265596
prince :
amen
2026-08-20 07:34:40
2
morieh26
memoh :
Amen 🙏
2026-08-20 04:30:51
2
To see more videos from user @kaybeste, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About