@anniek1996:

Anniek1996
Anniek1996
Open In TikTok:
Region: ZA
Thursday 20 August 2026 10:06:14 GMT
138294
5417
1682
595

Music

Download

Comments

mwayitembo253
natenasu tembo :
basi ngati muona kuti ife aseveni tili oipa inu kayambitseni mpingo wanu ife oipafe tikhala
2026-08-23 03:31:57
1
cathyjay83
cathyJay :
Ndie kuli ife amboni za Yehova timazitamandira ngati kuti Yehovayo ndi wathu ekha, makaninso ndi anthu sitimva zamunthu😊
2026-08-21 07:04:47
152
nestedkhembo
nestedkhembo :
Well said, sister. Truth will set you free. Kunena za anthu ena kapena mipingo ya ena sizingathandize kukapulumutsidwa kumwamba. Do what God wants. Tawonga, sister.
2026-08-22 06:56:41
1
user8591702042410
Collins :
siiweyo koma mzimu wa Yehova wakuululira
2026-08-20 17:39:51
45
isabelthaundi
Isabel🥰 :
🤣🤣🤣🤣Ex wanga samadya zoletsedwa koma cheated on his wife with me
2026-08-20 16:57:51
114
sarahmvalo
Rudo Sarah Mvalo 💕💕 :
As a former Adventist. Munthuyu sakunama.
2026-08-21 22:01:49
4
nature..lover18
❤️💞 :
Nkhumba samadya koma akazi ayeni amadya
2026-08-22 04:45:52
16
nafenkhoma0
Charity💕 :
ndipo or maulaliki awo every Saturday kumangonena za amzawo
2026-08-20 20:08:48
41
rachaelmhango5
Racheal kalawa :
exactly we always go kukajeda ma church ena makamaka Roman Catholic Kaya anatilakwila chani Kaya
2026-08-20 16:56:07
68
jacquemogha
jacque :
izizi zumveka ngat zamisala koma ndichilungamo inenso ndimpesa koma the way mmene anthu timaweluzilanaa eeee can make some one kuzimva kuchimwa💔
2026-08-20 22:34:57
19
cbl.chingondora
CBL Ching'ondora :
😂😂😂😂 kd ndimaona ngt ndimaona zimenezo ndine ndekha tuu
2026-08-20 14:54:33
20
alufisha265
Ken Alufisha Chinangwa :
CHIPONGWE ANANDIPANGA MKAZI WA AY INEYO🙌😭😭😭
2026-08-20 13:31:11
40
angetile6
Angetile :
ndipo ndipo sukunama
2026-08-21 10:27:02
1
paulineketie
paulineketie :
don't generalize....enafe we SDA kma we don't do that....izizi mungofuna anthu atinyoze
2026-08-20 22:53:29
8
cathykachipande
Cathykachipande :
ndiye powauzila anzanu a 7 wo ndipanopa?
2026-08-20 17:24:40
14
gift7937
Gift :
kuyankhula komveka bwino uku
2026-08-22 05:20:25
1
tkay_technician
Tinkie :
sda Yake iti imene mumapanga zimenezo? kwathuku ai.. even ma member fe timazimva kuchimwa kwambirinso.. abusa athu ndi atsogoleri athu samaweluza aliyense.. they will call a spade a spade but they will always be inclusive when doing so .. coz we are all sinners before holy Jesus Christ. kwanuko konzani machitachita Anu ndithu
2026-08-22 04:00:13
5
shepherd980
mother of 4 :
umamwa energy drink? on my bill dear
2026-08-20 18:52:14
5
daudi.banda7
daudibanda68 :
Si WA S D a ameneyo mumvele mayamkhulidwe akeo Ali ndi mpingo wake ameneyo siku Lina atchula mpingo wake ameneyo
2026-08-20 21:15:20
12
mathias.mlenga
A Mwale 😀🇲🇼 :
Kuteloko ayamba kukusala kamba kodzazdidwa ndi nzimu wa chilungamo... at this hour 😂
2026-08-20 17:08:39
7
user8842413250770
Dria patel ♥️🫂 :
kaya zanu zimenezo..SDA forever
2026-08-20 14:55:10
11
jolamu19
Jolamu :
Ine pano weni weni mpesa km mmmmh ayi ndithu ndipo wsndiyankhulira mah🙏🙏🙏
2026-08-20 17:19:33
5
judytoyasokosoko2
JUDY~TOYA🌸🇲🇼🇿🇦 :
Ndipo sukunama eeeeee seventh day 🙌🏻🙌🏻
2026-08-20 16:05:48
5
chriss5628
FAKE LIFE :
pano ku church sikumandisangalatsanso nkhan zake zimenez, MULUNGU atithandize
2026-08-20 18:22:17
10
ziowasaidi
Zio Wa Saidi🇲🇼🇿🇦 :
Amen 🙏 ngat ndimpange tag wina wake 🤣🤣
2026-08-20 10:57:06
9
To see more videos from user @anniek1996, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About