Apa wapala brother zogula anthu alindalama zopanda ntchoto
2026-08-21 15:26:26
0
JUMA MHANGO 🤣 :
🤣🤣🤣🤣 Lumbani khala serious please
2026-08-20 19:31:54
0
MULUSU CARPERNTRY AND PAINTING :
amene agule galimoto iyi a Traffic azikayankhula nawo chomcho😂
2026-08-21 11:06:30
4
Pastor Gift Gunundu :
inuyo bwana mukhoza kupangitsa kuti munthu ugule ngakhale tayala lokha la galimoto kkkk Mulungu anakudalitsani ndi mawu achilimbikitso kwambiri you are so blessed kuitanila malonda, God bless you 🙏 🙏