@anniek1996:

Anniek1996
Anniek1996
Open In TikTok:
Region: ZA
Friday 21 August 2026 08:31:19 GMT
53871
1761
594
87

Music

Download

Comments

candipriowethu95
Lady T Raps 95 :
Zindikilani kuti adani ozaononga mpingo sikuti azachoka kumipingo ina nooo azachokela nkati momwemo,,tili mu nthawi yomaliza musaope munthu wadziko inu kozani ubale wanu ndi Yehova koma ndingokupemphani kuti muchenjele mayankhulidwe coz mukusekela anthu ena kunja🙏
2026-08-22 15:11:12
2
4321mercy
mercy🌟🤩 :
i new kut ena akwiya nazo mix ziko lapasi limadana ndichilungamo
2026-08-22 21:37:28
0
thehomie118
Mwai_Yourhomie :
Ine anandiyatana ku service. They were referring to us a mipingo Ina as “ anthu a Chikunja”
2026-08-22 08:13:05
1
abiti8395
abiti :
Ine ndi WA CCAP ndimafunitsitsa ntalowa SDA koma simmene amaweruzila zimadzandibwenza mbuyo. I just resorted to listening to SDA songs basi. You are right baby girl
2026-08-22 10:16:08
6
susanpaundi142
Susan Paundi :
ineso ndi wa SDA,anthu ife ndioziyenereza,palibe chomwe walakwisa,ma elders wo akhale munzimu wakuweruzika,ine ndinamva bwino ndipo ndinszivomereza
2026-08-22 05:52:03
3
boldwinmakalani6
boldwinmakalani6 :
don't apologize for the truth
2026-08-22 04:14:18
2
user3063949086708
Christina Chanza :
ndipo ife a SDA ndife anthu oipa ozikonda
2026-08-21 11:55:46
41
naliwa
user1030580993154 :
Ndipo osachotsa inenso ndi wa SDA koma ndife anthu ozikonda
2026-08-21 11:34:55
68
stevenmatewere
Steven Matewere :
Mayi panalibe cholakwika ine ndi wa SDA koma munayabkhula zoona
2026-08-21 18:10:58
29
lourin4301499932923
Lourine4301499932923 :
sister osadandaula uthenga uja umapita kwa mipingo yambili amene yamupweteka ndekuti amachita zimenezo osaopa nkhani ndiyoti asinthe asamangosala za kudya ndi kusunga sabata km alibe chikondi 🤣🤣🤣 yabaya kod ulemu wanu sister ♥️💯💪💪
2026-08-21 11:10:48
28
user99353705234097
Holiness n Clara :
konzani ubale wanu ndi Mulungu, mukalimbana ndi gulu muchedwa nduona ngati.
2026-08-22 13:07:24
6
gracekamanga4
Grace :
komanso ndekuti mpingo sufuna kudzudzulidwa nanga video ija inalakwa chiani kuti ena akhale offended
2026-08-21 18:20:32
17
shepherd980
mother of 4 :
ndipo anthu mmadzikonda inu ine ndi wa ccap koma ndimatha kumvera nyimbo za SDA koma iwowa suzamva akumvera nyimbo za mpingo wina
2026-08-21 18:43:46
11
user8228863599221
𝓖𝓻𝓪𝔂 𝓶𝓪𝓼𝓲𝓶𝓫𝓮 :
ndiye vidio imeneija or atafufuta ine ndidzaiponyaso chifukwa ndaipanga save
2026-08-21 15:49:10
12
user3173983511229
user3173983511229 :
ndipo ndi zoona inenso ndi mpesa omwewo koma too much kuweluza
2026-08-21 11:40:58
10
alicegeordan
faith :
ndinapitako ku SDA tsiku lina koma ife ma pente nde tinanyozedwa mmmmm ndinachita kuzimvela chisoni kuti kodi ndimabweleranji kuno
2026-08-21 14:19:13
13
user8657965734782
Grace :
And iqoute"video ili pamalo pake"
2026-08-21 18:24:07
5
getrude5639
getrude :
musachose mama munala lakhula chilungamo ziwani kuti chilungamo chomawawa musachose please
2026-08-21 11:07:36
7
joyce.mtaya
Joyce Mtaya :
Ndekuti mudanena choonadi cc nanga chokwiyira ndi chani mulungu amawona mu mtima osati Mpingo
2026-08-21 09:40:36
7
kholiyokondwani
Manuel Kholiyo :
😊😊😊😊siwe phesa ayi
2026-08-22 01:04:59
0
user4572451266797
Henz :
big up 👌
2026-08-21 19:00:28
0
whizdavies
whizDavies :
Zaziiii
2026-08-23 05:22:30
0
efridaphiri886
efridaphiri886 :
akulu palibe mpingo wolungama tonse tili pachisime cha bethseida even kwina munenako kuli mabvuto awo sangakuzeni iyayi amadzudzulana kumbaliko nkhani ndiyoti inu kharani wa SDA woyenerawo kuti anthu mwa inu asaonemo kuweruza koma chikondi...Ku church ndikuchipatala ena amachira ena ai...if you expect to find good people only Ku church then sizingatheke even pa ophunzira a yesuyo panalinso wakuba
2026-08-22 16:56:27
0
pamnakoma08
Pam :
mwandiyankhulira I went to a certain church just to pray with them aaa koma kunanyozedwa mpingo wakatolika ine being wa katolika after ulariki mnangotuluka ndipo mnaziuza kuti ine nkuchimwa kwangaku sinzapitanso ku church kwina olo ntapangidwa invite
2026-08-21 18:18:20
3
daisley5
blessedgem :
kukula mtima ndikomwe mlinako
2026-08-21 13:11:31
4
To see more videos from user @anniek1996, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About