@history.guy04: The story of Marshal the dukes

THE HISTORY GUY
THE HISTORY GUY
Open In TikTok:
Region: MW
Friday 21 August 2026 17:48:52 GMT
25378
844
72
71

Music

Download

Comments

user6147095171983
Trust :
aaaa Kodi masho amkatiopswezera makolo uja ndi uyuyu?
2026-08-21 19:42:02
1
carosbranker
edwardmalunga :
Anali munthu wabwino ndinkasewela ndi Ana ake pamodzi ndi Ana a Likonde Aka Raster Du, amagula zinthu za tonse osa sankha kuti enafe tudzangosewelako. Oliver and Akim used to dance mu band yake b4 kupita ku zembani.
2026-08-21 20:53:49
1
..anabanda
Maa Nthanda :
Marshall ndi uyuyu Kodi...mesa ankati amapha anthu ..ife ankatiopseza akangoti kubwera masho kumakhala kuthawa
2026-08-21 20:27:25
1
brendamtandula
Brenda :
Ndikwa Samu osati Semu masho anali wamudzi mwakwathu kwa Mpingu
2026-08-21 20:51:30
1
nancy.salon7
Nancy hair studio :
First time hearing this Kom from the comment section it seems Ambili amudziwa 😅
2026-08-21 20:29:02
2
user81348884692985
Hosana :
amati kwa Samu Osati kwa semu
2026-08-21 18:25:56
9
ngoniyao
Ngoniyao Nels Ellias :
This is true 100% ife sitidamuonepo koma atafa kale tikangova kuti masho timathawa
2026-08-21 18:23:36
9
drkenamu
Enlyn :
Dolo uyu anali opoila kwambiri. He made Lilongwe a scary place to live in.
2026-08-21 19:15:22
4
nambe322
NAMBE🇲🇼🇿🇲 :
Kodi etiiiiii history Is the best teacher
2026-08-21 20:19:27
2
harrietkondowe1
Harriet kondowe :
ndipo tathawa 😅😅 mkulu uyu mmmm anatizuza
2026-08-21 19:54:12
1
user390426153195
Clara :
Kod uja amapha anthu?
2026-08-21 19:35:18
1
user7012980419476
pretty 🥰❤️ :
musandikumbutse ine kuchilinde akangodutsa eeeeee aliyese kuitana mwana wake amwene 🤣🤣🤣🤣
2026-08-21 19:54:03
1
b.kellah
beekay2012 :
amene akufuna mkamulozere komwe amkakhla masho, kwa biwi andipeze mmawa
2026-08-21 18:50:59
1
zakaahmbulaje
Zai thwah😂 :
live,ndipo kungonv Marshall akudutsa thupi limazizililatu
2026-08-21 18:33:54
1
chikonzerokasinj5
Chikonzero Kasinjah :
ndipo big mana makwanila inuo
2026-08-21 18:00:02
1
danielkabala253
Daniel :
kale nde kunali ma guys ogona pano tikana mu koza
2026-08-21 18:59:13
0
lu1tha94
@lutha94 :
kkkkk
2026-08-21 18:30:01
1
levizai5
Kammalunje :
history is the best teacher
2026-08-21 20:47:49
0
george.gp41
George Gp :
ifeso kwathu ku dedza tikangov dzina limeneli timathawa kukabisala
2026-08-21 20:30:58
0
user18234086182345
Andrian :
🤣🤣🤣 ku Blantyre kuno tingati ndindani ameneyuu🤣🤣?
2026-08-21 21:07:01
0
meyd36
mr mk⚡ :
uyu anali muthu okupha 👍
2026-08-21 21:26:15
0
falesipaul
FALESI PAUL :
Timaopatu
2026-08-21 20:40:00
0
calvin9856
Calvin :
timati kwa samu kwa mpingu not sem
2026-08-21 20:43:17
0
maryshadreck0
Mary shadreck :
ati chinali chigawenga ndithu
2026-08-21 18:42:25
1
To see more videos from user @history.guy04, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About