@preachwise: MAKONDOMU SANGAKUTETEZENI, TAVALANI ZIDA ZA MULUNG #gospelmalawi🔥🔥 #revalexanderkambiri #marthakwataine #revyasingama #preachwise

Preach Wise
Preach Wise
Open In TikTok:
Region: MW
Saturday 22 August 2026 08:06:48 GMT
100848
3746
397
845

Music

Download

Comments

chicco.szobo
CHICCO MASID📌 :
AA zazii apa mwasiya kukamba zauzimu mwalowa zakuthupi n kulimbikitsa ma Plein asa💔 verse yanji mwat
2026-08-22 14:38:10
1
mehek3415
mehek :
ma plain omwewo kuti WA WA WA🔥
2026-08-22 12:56:35
6
benjaminchris986
BENJAMEN CRISS :
bible says mkazi akhare chete pamaso pa mpingo so zolalikira azimayizi nde zichani
2026-08-22 11:08:05
5
bridgetch3
sisteri wamwana kale :
chokoma chasala ndichigololo chomwechi
2026-08-22 10:46:46
0
charity.beib87
Charity beib🌿🍒❤️🥰 :
Nd chapter chanj chmenecho
2026-08-22 09:50:58
0
malamaunda3
Tadala🦋❤️ :
koma akhale ma plen omwewa eti mah?
2026-08-22 09:55:50
40
user34266797268324
Joel Nkhata :
mai tangolalikani zamu Bible siyani za dziko
2026-08-22 10:52:42
15
victoriashanga3
Victoria shanga :
kod uthengawu uti chani sindikutolera
2026-08-22 11:00:31
2
user2498122606615
John Kay :
tiuzen uthenga wachipulumutso mama izi ayi
2026-08-22 09:50:32
26
grecianmthethwa
grecia :
athu awa ndi omwe amawanamiza athu kenako atenge matenda
2026-08-22 10:38:13
7
shantelstephanomchibwe
Shantel mwana sena,🇲🇿🇲🇼 :
unthebga uwu munali zophidzitsa kwambiri,koma ana anjoka inu mwangisakga apa cholinga mumunyozere zimayi uyu, mudzikuwopa kumbamba, mupite ku YouTube mukave uthenga onse mukavetsetsa
2026-08-22 10:03:00
9
trevormwamadi389
Mwamadi265 :
basi tizipanga ma plain
2026-08-22 09:38:47
11
useresther1238
user@esther❤️naphie :
osalalikila zaufumu wakumwamba bwanj ine maulaliki awa amandibowa nsaname zitipindulira chan iziz
2026-08-22 11:07:10
1
tamala301
Zoe🥰 :
By fire by force, osamalalikila moopseza koma. Ulaliki uwuwu kumuwuza munthu oti Ali mu zomwezo mkovuta kumusintha. Pepani ngati ndarakwa
2026-08-22 10:04:15
7
corrinee_00
🎀corrinee🎀✨️ :
what church is this?
2026-08-22 15:05:34
0
trizahtrix.banda
Trizah,Banda🌚 :
Inu munayesapo kutelo?
2026-08-22 11:08:18
0
annies939
Anita :
Ndinu a Hule
2026-08-22 13:27:26
0
wnyirenda147gmail.com
SmileySalo :
kodi condom ndiyoipaso?nanga tizitani?
2026-08-22 11:18:21
0
berthamsanu
Nyamwale💖 :
basi tizikwapulana Ndenge Ndenge
2026-08-22 10:32:37
0
masterkananji1
masterkananji5 :
inuwo amenewo experience imeneyo 🤔🤔
2026-08-22 10:43:20
1
dovouriaamae
Amanda#J J Twins :
tidasiya makondomu mai ndegendege pano
2026-08-22 10:51:57
3
mwayi.banda69
Mwayi Banda :
kod ndi verse yanji imeneyo 😂😂
2026-08-22 09:35:48
3
brhkmp
brhkmp :
apa nde bas ma plan andyanja nanga zikusyana
2026-08-22 10:27:05
1
user8573427062743
fronce harry :
ndikufuna uthanga wamulungu kt ndisithidwe muzimu izi ayi
2026-08-22 13:17:25
0
To see more videos from user @preachwise, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About