Well spoken brother, no jealousy. Izi ndi zomwe zimafunika kugawana nzeru, in so doing our country will prosper 🙏
2026-08-29 10:31:15
2
Thomas Gondwe :
zikomo kwambiri Bwana koma ndikufuna ndimvetsetse mwati madeya ampunga matumba 7, madeya wa chimanga 7,matumba a achimanga 10 koma matumba adeya 7 ndi ati? for madeya you have mentioned twice different rations 7 ndi 10 onsewa ndi achimanga ? clarify more on this
2026-08-29 16:03:06
0
Charles Gauti :
inuyo mulungu akupatseni moyo wautali ndithu, ineyo ndimaphunzira zambiri kuchokera kwa Inu, ngakhale ndili south Africa koma ndimalimbikisika kwambiri
2026-09-21 00:55:28
0
Misheck Chapomba :
ndikubwera tuuu April ndizayambeko ulimi umeneo
2026-09-03 15:51:50
0
georgemadeira2 :
soya fufeti mumapeza kt ndili Zomba
2026-08-30 19:43:33
0
Stacy_CL :
Ine nde daily pano ndimaphunzilapo chinthu china chake …..God bless you sir