ine aprophet ndinarota ndikugwira somba sikurina ndinarotandikuthamangisidwandi ng,na
2026-08-30 09:57:17
1
@mashilu Soko :
amen and amen Ines abusa kambiri
2026-08-31 19:44:03
0
felina beab :
ine ndinalot ndilikumalawi koma panopo ndilikujon ndie nditafika ndinayamba kukunkha chimanga maminda mpaka enaso anayamba kundisilila kuti ifeso tikayeseso
2026-08-30 10:35:50
0
Maria Mdutu :
Jesus is lord
2026-08-29 22:52:17
0
Freciano jovecio :
Ine ndinalota ndikuyenda pamwamba pamadzi zimatathauza chani abusa
2026-08-29 21:40:06
0
glory jere :
ine kulota ndavurara mwendo kuzukadi ikupezeka matupa komaso kuwawA
2026-08-30 11:13:43
0
Far beib Sandlam :
Ambuye atithandize and apitilize kukusogolelan pa utumiki wanu🙏 . ine nalota Gold akuchokela kumwamba nditamuwakha mmanja mwanga then ma key zonse mkuziwakha km tinalipo anthu ambili ndimaziwina ndekha ose kuwawuza palibe amaona kd mungandithandizeko kuti dzuthandauza kuti chan?
2026-08-29 18:11:41
1
user75026857483921 :
Amen
2026-08-31 11:56:03
0
Samuel wa kayele :
ine nimagona nimalota ndavala uniform ya scout koma ndisebenza pa loge ina ku zambia
2026-08-29 19:09:15
0
Frank makina :
Ine mdimalota bambo anga atachitidwa chiwembu
2026-08-29 19:04:16
0
Tiyanjane Millionmoyo :
Amen and amen
2026-08-29 19:09:56
0
fatimah :
ameni pastor
2026-08-30 17:20:20
0
Tenique Alexander :
Ambuye atithandize
2026-08-29 17:28:34
0
Emma1122 :
ninalota wakufa anipasa ndalama
2026-08-29 18:47:39
0
Bhullie :
Prophet Ine ndikalota kalikonse kakumachitikadi ndendende mmene nnalotera,,,
2026-08-29 18:53:37
0
AISHA FRANCES :
A prophet ine kupasidwa nsalu nd wa misala kms ndkakumana ndwamisa amandtenga ngt nzake kwambr km nthaw zambili kumakhalila kumulota mamuna ot ndnasiyana naye zikutathauzanji?
2026-08-29 18:35:56
0
Black child :
ameni
2026-08-29 18:58:18
0
Hope Kapele :
amen
2026-08-29 19:50:29
0
gift wa yacobe :
ninalo lota ndlnd graduation ku universty km ndl ku sekondary lelel
2026-08-29 19:18:42
0
Jolie baby :
please help Mamie anga akumalota athu omwe anafa kale kale ndipo akumakhala moyo ndikuyamba kudwalanso ndikufa please help me amalota tsiku ndi tsiku