zikoma ya hallah pondipanga kukala silami amene🥰🥰🥰
2026-09-28 11:51:12
0
mercychidzukira :
ine uyamba kuva chiphuzitso chako ndinadziwa ndiwe wa church of Christ.amayo ine kutuluka mpingo wa yesu nkukalowa wa ccap cifukwa cha banja
2026-09-29 08:39:32
0
Mada Mizere39 :
mpingo ndwa seventhday adventist basi
2026-09-28 11:10:07
2
Arthur :
Solomon was a magician.
2026-09-28 13:42:15
0
Mc Ben Ntapo :
Zoona zake
2026-09-28 14:33:57
0
Cle John :
Vuto sudziwa kuti SDA ndichani
2026-09-24 17:01:32
1
Madaritso Twahaa :
nde pingo wowonawo ndi ndiwuti???
2026-08-29 23:38:02
6
devies jasten :
ndipo live bro ine ndi wa church of Christ bwanawe
2026-09-26 19:25:49
1
James Nkhata :
Mpingo woona ndiymozi okha mpingo wa yesu basi
2026-09-24 15:50:04
1
ellenchipojola2 :
mpingo ndiwomwewu wa church of Christ
2026-08-31 15:23:48
5
Adchang 13teen :
If not sda mpingo wina ndi uti CHIVUMBULUTSO 14:12 Pano pali chipiriro cha oyera mtima, cha iwo akusunga malamulo a Mulungu, ndi chikhulupiriro cha Yesu.
Chichewa bible
2026-08-31 05:03:58
5
Raphael Soko :
Mpingo kutchedwa Church of Christ sizithauzakuti ndinu oona Yesu anachenjeza kale kuti sionse akuti Yesu Yesu akapulumuka
Zoona zake amen Ambuye akupasani mavumbulutso ochuluka brother angakhale nthawi ya yesu si onse amavetsesa
2026-09-06 11:11:06
1
Sosten Wailes Yusufu :
m'bale fundo zanuzose ndikuzitsata bwino zedi, koma chithu chimodzi pewani kulakhula moweluza pakuti kuweluza kuli kwaiye mwini, koma kwina koseko zilibwino ndipo mupitilize ambuye yehova akusamalireni.
2026-09-14 02:35:26
0
DONNEX KHAMA :
powerful zikumveka louder and clear
2026-09-24 09:47:42
1
Charlos Gama :
mtumiki ameni mundipatse #yanu
2026-09-01 10:02:25
0
Thomas Masina :
Church of christ
2026-08-31 15:05:50
4
Samuel Mw :
amen and amen, ndizoona
2026-09-15 05:17:17
2
Linnie :
nde zingatheke kut dziko lose tikhale nd mpingo emozi komaso there's no way or ku SDA azipanga encourage ntchimo and anthu they sin not because ku church kwawo akuwapanga encourage and of course tikapulumuka mwachisomo not because of a church