abusa ineyo ndakonzeka kumusatila ambuye yesu ndi mzimu wanga onse please ndithamdizeni ine , ndilimbikiseni pandekha ndilephela chonde, ndikadakhala pafupi ndikwanu ndikadajoina church chani koma from today please be my spiritual father, chonde chonde 🙏😭😭😭😭😭
2026-09-17 16:55:46
0
kingsly musemo :
iuzeni zoona
2026-09-18 20:07:48
0
Getrude Majawa :
ndizoonadi
2026-09-27 07:55:54
0
Megrina :
zoonadi anthu ambiri akufunazozizwa koma zotiakoze mitimayawo pakuti mulungu anenakuti mukakhala mwa ine sungani malamulo anga abusa pitilizani kuwauza choonadi athu akusochera
2026-09-23 05:14:52
0
user6003701291202 :
zoona
2026-09-21 05:24:33
0
Lucy Julius hesi junior :
amen amen papa zoona🙏
2026-08-30 08:46:28
2
Moses Makuwira271973 :
Amen 🙏
2026-08-30 08:48:40
2
piliro :
amen
2026-08-30 09:14:27
2
EDHO KAY NKHONDE :
amen 🙏
2026-08-30 12:45:44
1
Simon Mawindoh :
Amen
2026-09-22 06:02:43
0
Levison Chilemba :
Amen
2026-09-17 13:26:13
0
Thokozan Tembo Mr Smart :
Amen amen
2026-09-24 17:13:30
0
Patshaza iphampasi Dayikuta :
Amen
2026-10-01 18:28:21
0
Ruth kachikho :
mulung andivele chison andithandize ine
2026-09-17 11:01:31
0
Mercy Nthondo :
Ndiwo zovesa chisoni ambuye andithandize
2026-09-17 04:53:15
0
Lester Duncan :
amen amen
2026-08-30 09:23:02
1
Francis Burton :
ndizoon thawi yathad mulungu atithandiz
2026-09-16 03:22:05
0
rhodrickndalama :
Amen amen amen
2026-09-16 02:22:15
0
elizabethphiri8168 :
nenan abusa amen 🙏🙏🙏
2026-08-30 09:41:05
1
To see more videos from user @apostlemilliondaniel, please go to the Tikwm
homepage.