@hedmannursery:

HEDMAN NURSERIES COMPANY LTD
HEDMAN NURSERIES COMPANY LTD
Open In TikTok:
Region: MW
Sunday 30 August 2026 09:12:47 GMT
177869
5279
278
555

Music

Download

Comments

user8552593693998
user8552593693998 :
Km family ya lucias why poul amalakwa chani
2026-09-02 19:34:32
0
gift.maniya
gift maniya :
Osadandaula kubwenzela ndi KWA YEHOVA, Mulungu akuona
2026-09-03 06:07:06
1
ashrafbanda14
Ashraf Banda :
kod anthu amaipa ntima ndikhope yomwe eti akuchikazi siyanthu alla
2026-09-03 12:35:26
0
chigho2
Chigho’s Beauty Bar😍❤️ :
I thought I saw Paul Banda pa chiliza.
2026-08-31 04:26:30
16
user1611869925772
mache :
mwana wa lusius ndi oyipa
2026-09-03 07:28:40
0
user1485380391693
Monica :
zomvetsa chisoni
2026-09-03 17:24:50
1
nkhudohnyamkamang
Nkhudoh Nyamkamanga :
mmmmmm...zomvetsa chisoni kwambiri....
2026-09-02 17:08:06
0
angel.gutah
Angel Gutah :
Malawians we are so kind we can do something for him
2026-08-30 19:54:55
51
sylviachilyaba
lij sway 79 :
Pepani ndinthu Mulungu akudalitseni pazabwino zotse mwankhala mukuchita, Mulungu salakwitsa
2026-08-30 16:43:12
13
user9498455791465
❤️alice@ :
amai muzawafuna akuchimunawa chimafuna china chake muzasowa kolowera nazro mesa muli ndiyana kuzimva kumeneko ulemu ndiwofunika mai
2026-08-30 19:05:39
20
resiyamakoloni
Resiya Makoloni :
anamalila amangolila nkumapita anamfedwa ndiife omwe tinaluza muthu yemwe tinkankonda ndipo timadalila
2026-08-31 07:49:32
11
mkaladiwabii
Mkaladi Wa Bii :
chonchi mzinu wa soja ungagone abalee??
2026-08-31 11:30:15
14
kabilamalimusi
Kabila Malimusi :
zamvela Kodi nanga ana a the late Lucius ali kumbali iti apapa
2026-08-30 20:37:16
19
lee.babie4
Lee babie :
amai ameneaja ndimkati ndimunthu kona ai chiserekwete chenicheni ndatulukaso apa.paul don't worry ndinachimwa poganiza ambuye mundikhululukire..
2026-08-30 19:36:34
8
user51972252578047
user51972252578047 :
asandukano agalu anthu akuchimuna aja☺️osamatero abale☺️
2026-08-30 20:46:12
6
gladyssendeza265
GLADYS :
Namadingo mulikuti brother timaku dalira ziyambitse anthu asokha
2026-09-01 13:19:21
5
matthewsaddam
Matthew’s :
Zomvetsa chisoni 😭😭tiyeni timukonde munthuyo Ali Moyo plz Malawias 😭
2026-08-31 16:43:16
9
user5144351900082
user5144351900082 :
kulakwatu uku
2026-08-31 05:37:14
5
ghiseramacdonald0
ghiseramacdonald :
Nkazi ameneyo ngwamwano, zikuonetsa kuti ngosowa khalidwe kuyambira kale, amangozibisa zakhalidwe lake ndiloyipa... ine kumbaliyanga ndikuona ngati Amfumu ndiinu nonse akumtundu mumusumire mkazi ameneyo cos wakudelerani nonse kumeneko, iyeyi anaganiza bwanji zotsegula kumanda popanda Amfumu? kuMlw kuno ndimwambo wathu kt tisanayambe mwambo ulionse okhudza zakumanda, timayamba kupita kukapempha chilolezo kwa Amfumu, Amfumu ndiomwe amatsegula khomo lakumanda... musamusiyetu choncho nkazi oyipa moyo ameneyo...
2026-08-31 07:25:04
11
user7920391369497
bella :
Pepani ndinthu koma Mulungu sataya wake
2026-08-30 19:46:45
8
mary.nellie.yasin
Mary Nellie yasin ganeth :
Azimai mmmmm 😭😭 chilipo chimafuna akuchimuna kuli ana kumeneko be careful azimai mmmm
2026-08-30 18:08:00
7
cmphambe22
chicco :
ine mkanakhala wakuchimuna chiriza chimenecho mkanatuma anyamata achigumure chifukwa apapa mkuderera eni mtundu nde kuti aziwe kuti munthu siwawo anangokwatidwa walahiiii nditha kuchisalazisapo kuzimva chani iyeyooo mpaka kuderera ndi amfumu omwe
2026-08-31 06:49:29
5
winniemzembe
Winnie Obeba💋💕♥️ :
my question!Kodi Manda angatsegulidwe amfumu osaziwitsidwa?
2026-09-02 11:14:49
2
To see more videos from user @hedmannursery, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About