@wanangwasam:

Wanangwa-Sam
Wanangwa-Sam
Open In TikTok:
Region: MW
Monday 31 August 2026 09:16:24 GMT
3123
81
15
9

Music

Download

Comments

user7579313183863
user7579313183863 :
zoonadi ndipo kunena zoona mavuto alipo siku ndisiku kugona mumdima Feteleza akuti tizigawana matumba awiri anthu atatu. sindinaone
2026-08-31 13:59:40
0
lasten.goodwel
Lasten Goodwel :
umasangalatsa kut unayankhula chilungamo koma azizako aku times chifukwa chabdyera ndi amene amapereka support kwambir kwa anthu amenewa
2026-08-31 15:05:02
0
user62461391123698
George Moses Chakhu Chinthalo :
Dpp on fire 😄😄😄😄
2026-08-31 11:18:46
0
user3716958206144
KAKHWESI :
True words Mr wanangwa
2026-08-31 13:10:42
0
nafebambo1
nafebambo :
Wanangwa I pray God protect you always. Ndiwe munthu wachilungamo
2026-08-31 16:26:25
1
dorothynkhonjera3
Dorothy Nkhonjera :
ndidzimene mukafuna mesa
2026-08-31 11:49:47
0
johnmainga133
Jumah, :
eishiii 🤣🤣🤣
2026-09-01 10:17:52
0
user556365087251
leeo :
mawu🔥
2026-08-31 16:11:40
0
zembe987
Zembe :
😂😂😂 Eeh
2026-08-31 12:14:26
0
user2046611993329
scofani bou :
mau koma amenewa
2026-09-01 03:43:35
0
saukanisinos
Mr S,sinos,chisaleKalonga :
achakwela waja sadaluze adaluza nd amalawi komaso pitala wagona tulo tofa NATO komaso ifeyo tidalakwa nde akuluwa adakula kwambiri adakalamba kwambiri sangapange za phavu 😳😳😳😳😳😳
2026-09-01 05:14:46
0
lasten.goodwel
Lasten Goodwel :
😂😂😂😂😂wangondiwaza poti mbisa wa ng,ombe akamagona ng,ombezo zimasokera
2026-08-31 15:06:46
0
dinachilima
dinachilima :
aPre agona ATI bola msima
2026-08-31 13:46:53
0
user9762679935312
so :
chuma chikuyenda bwino kubomakotu osati mmakomomu asaname,anthu alibe ndalama,anthu asauka kwambiri pano,alimi akulephera kugula feteleza..
2026-08-31 16:36:38
0
missionmassion1
Mission-Massion 1🦋💍🦋 :
🔥🔥🔥
2026-08-31 11:45:25
0
To see more videos from user @wanangwasam, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About