Auntflo2001 :
Chonde tiyeni tipange share video muma group onse, mumagroup aziphwisizo, kuzintchito, kuma group a biziness, ku chalichi chifukwa machalichinso akanikaa kusova ma issue aziphwisizi, kwa DC, ma MP, Radio Station, Brian Banda akanakhala ndi moyo, mmzimu wake uuse ndi mtendere, koma timuponyere, Joan Chakaza, Mibawa TV, Civil Society Groups, ma lawyer-umbuzima, mu ma khoti kuti dziko limve kukula kwa kufuula kwa azimayi kuno ku malawi, amene akukumana kapena anakumana ndi issue ya ziphwisi. Tsiku lililonse tiziposita kuti wakumva am ever, awa nde ma Demo athu.
2026-09-01 02:45:58