@user6706386240651:

Moses Saka Nyirenda
Moses Saka Nyirenda
Open In TikTok:
Region: ZA
Monday 31 August 2026 11:55:02 GMT
82489
4900
973
575

Music

Download

Comments

ness.ky5
Ness K@y :
kuumila bwino
2026-09-14 18:57:49
0
user805457107281
Maggie mw💪💜💜💜🇲🇼 :
Koma rero kwakoma ndikuno 🤣🤣🤣🤣
2026-09-14 17:30:54
0
violetnjoromore
Violet Njoromore :
umwa chani brow 🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳👊
2026-09-14 12:48:39
0
natashsangala
Natasha :
ndipo inu m
2026-09-13 19:53:02
0
shadaihbeib
SHADAIH :
Uli kut dear amene umazilipilila wenkha ma Bill 🤣
2026-09-01 05:02:33
189
riananelo
Riana Nello :
😂 😂 Okay to my status again 😂🤝🏻
2026-09-13 11:16:06
0
user2553092778174
chiso beaib :
mmamuna wandan uyu
2026-09-13 06:10:30
0
pat7005
pat7005 :
vuto rake ndikaika ku status adziona ngat ndkunenea iyeyo😂
2026-08-31 17:57:10
59
monicasakalaka
Monica Sakalaka :
straight to my status ...yobu 13:13🤣
2026-09-01 18:37:28
28
prince.zahier
Prince zahier ❤️ :
😅😅😅Ndayamba kukukondan
2026-09-12 17:44:20
0
user456156174
Godrich Ck the plumber :
Tionetseni akaz anu apa tione mmene mumasamalila
2026-09-07 09:24:59
0
testimony831
char :
ine or 2pin sangandigaile dish🙌🙌
2026-09-09 10:29:36
0
promisejele1
promisejele756 :
amuna anga akadaonako video iyi coz ndikaika status akuchimuna andiluma🤗🤗
2026-09-02 05:18:16
5
aminamwenyeku
Amina Mwenyeku :
Ine ndiyika ku status 😂😂😂 osamaopa girls 4n ndi yanu let's go
2026-09-01 19:25:33
7
cute.faith30
cute faith 💝💦 :
Mamuna uyu kaya ndikutani naye ine 💔💔
2026-09-02 09:22:12
0
user9211761901978
Gospel :
😆😆😆😆 Kma na mamuna wanga eeeee ulemu wake sadikila umupemphe amangokupangira yekha
2026-08-31 18:49:14
7
user774041338518
user774041338518 :
kkkkkk! mamuna oti nthawi zonse ndabalalika ndimaproject or khodo kkkkk😂😂😂😂😂
2026-09-01 14:26:12
6
aliyah.adamu8
Aliya hamudn :
zili kuno ine bas ndichok bola zikalima aaa
2026-09-01 08:50:55
11
patricia.soko2003
Patricia soko :
wa ku status 🤣
2026-09-01 11:03:06
1
user217148346132
@sarrahmalupi :
Koma ine ndye sindnganame mulungu azimudalitsa mamunayi
2026-09-11 04:21:20
1
user27035786904068
Juliette Longwe :
🤣🤣🤣 umwachani broooo
2026-09-05 15:01:16
1
chimamichovuta
Mamie💝 :
kod chimamuna ichichi ndikutani nacho ine
2026-09-01 13:23:18
2
ulemumanda586
ulemumanda586 :
koma ndipo zoonadi
2026-09-01 12:01:40
1
xaviermafubza4
Eve Naphi :
volume yatsika kwambiri...kwezani bro😁
2026-09-02 04:20:57
1
english.explorers180
Sir Michael Kings :
Abambo inu ndiopusa! 😂 Mukupereka chilichonse kwa mkazi chifukwa chofuna kumva kuti, “Wow, you’re such a good man.” Mukufuna applause mpaka mwaiwala kudzilemekeza. Dzukani! Kumuchitira mkazi chilichonse sikumamupanga kukhala wanu. Tsiku lina akhoza kungonyamuka ndi zomwe mwamupangira, n’kukusiyani mukuyang’ana denga. 😂🔥 Mkazi wa “look sharp” akhoza kugwira ntchito, kupeza ndalama, kusamalira nyumba ndi kupanga moyo wake popanda kukhala dependent pa mwamuna. Ndipo mwana wanga wamkazi sindidzamulera kuti azifuna mwamuna kuti akhale complete. Ndimuphunzitsa kuti akhale ndi nzeru, ndalama, confidence ndi mphamvu zake. Mwamuna akhale bonus m'moyo wake, not the whole life. Ndipo ngati mwamuna wachoka? Moyo ukupitilira. 💀🔥
2026-09-05 18:04:48
0
To see more videos from user @user6706386240651, please go to the Tikwm homepage.

Other Videos


About