ndabwerako koma who am I to judge... tsikana uja anamutenga Ali mwana nzeru zisanakhwime he manipulated her olo kumumangilako manyumba mu area mu Inu.. kulakwa
2026-09-02 14:25:09
55
Psalm 34 💕👌😍 :
komatu ine ndaphuzilapo something be financial independent muchilichose
2026-09-02 13:33:42
136
Jayne Jaydacris Chapomba :
zabodza inu we should hear from Abidas side. last time I checked anachita kumuthawitsa sidik after the wife found out.
2026-09-02 15:08:05
11
Tamar Pemba :
Ati asamapange chilichonse chifukwa ndi mkazi wa minister 😭💀but the VN’s that leaked weren’t they arguing about child support? With the late Mia
2026-09-02 14:13:55
18
Tee-KayEL :
kenako mkuzat iyayi samadziwa kut tinakwatirana😂
2026-09-02 19:08:42
0
MAKESHEBA :
ineyo financially ndine DOLO woth the little i have ... anthu mukugwira ukapolo pakati pa miyendo!
2026-09-02 18:57:50
2
millen402 :
Kodi ukuti chani
2026-09-02 13:19:51
4
nthandosiSilungwe :
Wayiwalanso ati school fees imalipira company yoti asisi ndi dzaddy onse anali ma signatory.
2026-09-02 19:00:42
0
madalitso vashie :
ndipo okumva wamva.😂
2026-09-02 19:01:31
0
zenithkulankwa :
ndiye iyeyo ngosqphunzira kod?coz apapa ndili ine ndiphunzirqtu mpaka phd😂😂
2026-09-02 13:53:40
5
ᒍᗩY ᖇ DaVinci :
Face 2 Face on youtube
2026-09-02 12:49:38
2
mrs banda ( MJ) :
yachitika liti iyi
2026-09-02 12:50:02
2
Memo❤️ :
😂😂😂😂😂izizi zikutipangisa kuti tizilimbikila
2026-09-02 18:15:32
1
robina khudze :
osisi tiuzeniko mukuti zili kutiko
2026-09-02 14:30:07
0
Michelin🎉 :
ndipo simene kulili🤣🤣🔥🔥
2026-09-02 13:27:01
0
Beccah Makuse :
zachitika kuti
2026-09-02 12:55:23
0
Naphi :
ine amuna motelo nditha olo kumunyambita nsete 😫 iiiih mpaka business class??😳
2026-09-02 13:38:30
2
patricia66923 :
she was happy that I was dating him 😂
2026-09-02 14:40:53
5
TheCutter :
ineyompaka ndakaonera full podcast after seeing this video😂😂😂 mumatha marketing🔥🔥😂😂
2026-09-02 15:16:13
1
Miss Handy :
My lesson is that as the man is alive let him put his house in order osati…..
2026-09-02 16:38:49
1
Claire 95🥰🥰🥰 :
Ndipo my question is panopa Alindi chani abale?
2026-09-02 13:18:28
3
To see more videos from user @swenga01, please go to the Tikwm
homepage.